Real Malawi Football News On-Line

Real Malawi Football News On-Line Trying to give the latest sports news around the globe to the people

Mphunzitsi wa Scorchers,Lovemore Fazili, wati ali ndi timu ya mphamvu yomwe ichite bwino mumpikitsano wa Women's Africa ...
24/07/2026

Mphunzitsi wa Scorchers,Lovemore Fazili, wati ali ndi timu ya mphamvu yomwe ichite bwino mumpikitsano wa Women's Africa Cup of Nations (WAFCON) ku Morocco.

Fazili wayankhula izi dzulo timuyi itagonja 4-0 ndi timu ya Ghana pamasewero otsiriza okodzekera mpikitsanowu omwe anachitikira pa bwalo la Municipal de Berrechid.

Doris Boaduwaa anamwetsa zigoli zitatu zomwe zinabwera mumphindi 8,37 komanso 47 ndipo Sharon anamwetsa china mumphindi 74 kupangitsa Ghana kuti ipambane ndi zigoli zinayi kwa duu.

Mphunzitsiyu anatinso anagonja masewerowo kamba koti anayambitsa osewera amene sasewera pafupi-fupi pofuna kuwayetsa ndicholinga choti awaone m'mene angachitire.

Iye wapereka chitsimikizo kuti ngakahale timuyi yagonja masewero awiri opimana mphamvu omwe Football Association of Malawi (FAM) inawakodzera ku Morocco chikhulupiliro alinacho kuti achita bwino.

Malawi ikuyamba masewero ake a mugulu C lachiwiri pomwe adzakumane ndi Nigeria kenako Egypt ndipo adzakumana ndi Zambia pamasewero otsiriza.

Charles Chipala, as the June Player of the Month winner, was presented with a K500,000 shopping voucher by our partners ...
24/07/2026

Charles Chipala, as the June Player of the Month winner, was presented with a K500,000 shopping voucher by our partners C.P Investments Malawi.

Below is a pictorial of how the forward spent his time at the multi-award winning fashion store on Wednesday.

🎢Tiadode Tiadode tikamaliza tiaphode, pamapeto akhale ma Banker!!🎢

Katswiri otchinga kumbuyo mutimu ya FCB Nyasa Big Bullets, Yamikani Mologeni wasankhidwa kuti ndiamene anasewera bwino k...
24/07/2026

Katswiri otchinga kumbuyo mutimu ya FCB Nyasa Big Bullets, Yamikani Mologeni wasankhidwa kuti ndiamene anasewera bwino kuposa aliyense mwezi wa June,2026 mu FDH Bank Premiership.

Mologeni wapondelera osewera pakati ku timu ya Civil Service United Righeous Banda komanso osewera wa Silver Strikers Innocent Shema.

Osewerayu anasankhidwanso kuti anasewera bwino mumasewero onse a league omwe timu yake inasewera mwezi wa June.

Potsatira kuchita bwinoku,Mologeni walandira ndalama zokwana K300,000.

kwa omwe mumazitsata bdi kuti uku?
24/07/2026

kwa omwe mumazitsata bdi kuti uku?

inu maganizo anu ndi otani
24/07/2026

inu maganizo anu ndi otani

International friendly results Dzulo usiku
24/07/2026

International friendly results

Dzulo usiku

πŽπ…π…πˆπ‚πˆπ€π‹ : Marie-Louise Eta will take charge of Bundesliga side Union Berlin until the end of the season. A historic mil...
13/04/2026

πŽπ…π…πˆπ‚πˆπ€π‹ : Marie-Louise Eta will take charge of Bundesliga side Union Berlin until the end of the season.

A historic milestone β€” she becomes the FIRST woman to manage a men’s team in Europe’s top five leagues!

Scorchers vice captain, Temwa Chawinga, was on the scoresheet as Kansas City claimed a 6-1 win over Palmeiras  to defend...
13/04/2026

Scorchers vice captain, Temwa Chawinga, was on the scoresheet as Kansas City claimed a 6-1 win over Palmeiras to defend the Teal Rising Cup in United States of America on Sunday.

This is Temwa 's first goal after a return from her injury.
chiphe ma teams

13/04/2026

Arsenal need only 3 wins to be the 2025/26 premier league champions,Manchester city can't win every game.
mukalephera chaka chino simudzatenganso maganaz aku Ghana k*k

13/04/2026

Assistant head coach of Mighty Wanderers, Nginde Mtetemera, has revealed that Peter Cholopi, Clement Nyondo, Dalitso Khungwa, and Timothy Silwimba are recovering well after being given four weeks off by medical staff due to injuries and are expected to be available for upcoming matches.

Nginde said the team is ready for Bullets in the Charity Shield game on April 18 and is gearing up for the new league season as well.

Wanderers finished their preparations for the FDH Premiership Competition, having participated in the Sapitwa 4 Bonanza tournament, playing against Bangwe All Stars, Changalume Barack's, and Fomo FC.
Meanwhile, gate collections from their game against Fomo were donated to Fomo FC since Wanderers had requested the friendly match.

The team has returned to Blantyre after their game with Fomo and will travel to Mponela on Tuesday for their training camp ahead of the Blantyre Derby.

Address

Snell Street House No42
Rustenburg

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Real Malawi Football News On-Line posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Real Malawi Football News On-Line:

Shortcuts

Share