27/07/2026
Malingana ndi nyumba zolemba nkhani zaku America timu ya Spain singapatsidwe ndalama zake zonse zimene inapambana itakhala akatswili a mpikisano wa FIFA World Cup 2026 chifukwa dziko la America lidulako misonkho yake .
Maiko amene mumachitikila mpikisanowu amadula osewela aliyese msonkho chifukwa wagwila ntchito mu dziko lawo ndipo Spain ikuyembekeza kuchotseledwa pafupifupi 15% ndi America pa $50 million imene inapambana.
dziko la pansilili mmanja mwa trump😢