Akaphale TV

Akaphale TV Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Akaphale TV, Sport & recreation, Durban.

Nkhani mu chichewaChristiano Ronaldo akuona kuti Karim Benzema asapite ku timu Al hilal chifukwa apangitsa kuti pasakhal...
02/02/2026

Nkhani mu chichewa

Christiano Ronaldo akuona kuti Karim Benzema asapite ku timu Al hilal chifukwa apangitsa kuti pasakhale mpikisano pakati pama timu monga Al nassr, Al ahli, Al ittihad komaso Al hilal.

Benzema akusewela timu ya Al ittihad koma chifukwa anamupatsa contract yosasangalatsa akufuna kupita ku timu ya Al hilal ndipo pakuonetsa kusakondwa ndi chiganizochi Cr7 sasewela masewelo alero apakati pa Al nassr komaso Al Riyahd.

*Akakhale TV*

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yamvana ndi Karonga United kuti itenge osewera wa United pa mgwilizano omwe utheketsetse b...
02/02/2026


Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yamvana ndi Karonga United kuti itenge osewera wa United pa mgwilizano omwe utheketsetse bungwe loyendetsa masewero mdziko lino la FAM likatsegulira msika wa osewera.

Mwale yemwe ali ndi zaka 27 zakubadwa adali otchinga pagolo odalilika ku Karonga United pamene pa masewero 28 amene wasewera chaka chatha mu TNM Super League, sanamwetsetse chigoli chili chonse pa masewero khumi.

Iye anathandiziranso timuyi kuti imalize pa number 6 pa mndandanda wa matimu mu super league.

Bullets yalemba patsamba lake la mchezo kuti ikuyang'anira mwa chidwi kuti mgwilizanowu utheke.

(akakhale Tv follow for more updates

congratulations manoma
27/12/2025

congratulations manoma

ambili mukufuna yaa uyuuLink to the comment box
13/10/2025

ambili mukufuna yaa uyuu

Link to the comment box

28/09/2025
wit naye akati ayipemelele๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
28/09/2025

wit naye akati ayipemelele๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Team ya mighty wanderes manoma tsopano yayamba zokonzekela zake mdziko la Botswana ndipo ndipo akulu akulu a teamyi ati ...
25/09/2025

Team ya mighty wanderes manoma
tsopano yayamba zokonzekela zake mdziko la Botswana ndipo

ndipo akulu akulu a teamyi ati zikuoneka bwino ndipo zonse zili mchimake

,,tayamba bwino zikukongola anyamata akuoneka aphanvu komanso achilimbikitso tikukhulupilila kuti masewelo amenewa tichokako ndi ma results abwino,,

anatelo a bob mpinganjila poyakhula ndi

tsamba lino


# football malawi

24/09/2025

we back to the action

27/06/2025

khani za lelo

kunena zoona JB samalakwa potukwana aboma
athu amenewa ndiopusa kwambili machende awo
zoona Muthu angamamenyedwe a police Ali pompo

asilikali Ali pompo ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ญ

koma ndidikile Kaye nditukwanabe wait.....

03/06/2025

This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.

06/01/2025

Mponda uja wapita

Apwetekana

Address

Durban

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Akaphale TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share