10/07/2026
Bible silimafunikira filimu... Anthu awo analakwa kwambri...
Palibepo Yesu apo... Chonde
Awa anali ma actor chabe.... Palibe mu generation yathu angakhale nd chithuzi cha Yesu...
Tizingowelenga Bible lo basi and kulikhulupilira... Osati kukhulupira mbuzi za anthu zili apozo
ð ð€ ð€