Sports desk

Sports desk Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Sports desk, Professional Sports Team, Chikwawa, Zomba.

LEAGUE  IDAKALI IYI INU Silver Strikers  have 2 game in hand✋️
29/10/2025

LEAGUE IDAKALI IYI INU

Silver Strikers have 2 game in hand✋️

  Timu ya mikango yofiira kuzomba yomwe ndi yachisilikari Red Lions ikuchita bwino kwambiri mu ligiyipakadali pano red l...
28/10/2025



Timu ya mikango yofiira kuzomba yomwe ndi yachisilikari Red Lions ikuchita bwino kwambiri mu ligiyi

pakadali pano red lions ikutsogola ndi mapoints 36 pamene yasewera masewero okwana 16

pambuyo pake pakubwera Baka City yomwe ili ndi 29 points pama gamu 16

Sports desk

throw back  January 5, 2024SINGINI AKUSAINA CONTRACT YAKE KU MANOMAAmbiri analankhula pachifukwa chaku munthawi yomwe pl...
27/10/2025

throw back January 5, 2024

SINGINI AKUSAINA CONTRACT YAKE KU MANOMA

Ambiri analankhula pachifukwa chaku munthawi yomwe player yu ankabwera ku timuyi nkuti wanderers ilibe coach aliyense. km pano ndi player odalirika kwambiri ku lali Lubani

27/02/2022


125minutes

Chelsea vs Liverpool
0_0

10/01/2022

1st eleven ya FLAMES


Ernest Kankhobwe

Gomezgan Chirwa
Limbikani Mzava C
Dennis Chembezi

John Banda
Peter Banda
Chimwemwe Idana
Micium Mhone
Francisco Madinga

Khuda Muyaba
Yamikani Chester

07/11/2021

Airtel top8


On 06november
NBB 3 -1 MAFCO

On 7 November
Mighty wanderers 0-1 Moyale barracks

14/04/2021

-resultS
Pa 14 April 2021

Mighty Wanderers 4-1 Ntopwa
Babatunde Hendlix
Wadabwa
Sanudi
Kaliat

05/04/2021

YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERS

Bungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu

Ndipo team ya dzikolino ya flames ili gulu(A) ndi mateam monga Mozambique, Cameroon

  YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERSBungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu...
05/04/2021

YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERS

Bungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu

Ndipo team ya dzikolino ya flames ili gulu(D) ndi mateam monga Mozambique, Cameroon ndi ena ambiriii

24/01/2021

Man Untd 0-1 Liverpool

19mns {salar}

  ZA MANOMA .........................................................Team ya Mighty Wanderers yayambaa zokonzekeraa zake...
06/01/2021

ZA MANOMA
.........................................................
Team ya Mighty Wanderers yayambaa zokonzekeraa zake lachiwiri week ino pokonzekeraa
game yomwe alinayo weekend pomwe akhala akusosorana nthengaaa ndi anyamata a Karonga United pa bwaro la KAMUZU STADIUM mu mzindaa wa Blantyre

Ndipo gameyi tizakupasiraniiii LIVE on sports desk(BEN MEKE)

Happy new year all members

Address

Chikwawa
Zomba

Telephone

+265883728625

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sports desk posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share