02/06/2026
Mwadzuka bwanji Anthu okonda masewelo kuli konse komwe muli
Bungwe loyendesa masewero kuno ku m'mawa dzulo latususa ndandanda wa masewero amu Division league 1( kale imatchedwa kuti premier Division league)
Ndipo chigawo choyamba chiyamba motere
Zomba Immigration vs Nsanama young soccer
🏟️ Police ground Zomba
📅 7 June 2026
🕛 2:30pm
Nsanama young soccer vs Ntaja Rangers
🏟️ Vision stadium Ntaja
📅 14 June 2026
🕛 2:30pm
Namikango Mission vs Nsanama young soccer
🏟️ Albright stadium Thondwe
📅 20 June 2026
📅 2:30 pm
Nsanama young soccer vs Kababa Academy
🏟️ Vision stadium Ntaja
📅 27 June 2026
🕛 2:30 pm
Toleza farm fc vs Nsanama young soccer
🏟️ Toleza farm ground balaka
📅 4 July 2026
🕛 2:30 pm
Nsanama young soccer vs Rutrand FC
🏟️ Vision stadium Ntaja
📅 12 July 2026
🕛 2:30 pm
Malawi Navy FC vs Nsanama young soccer
🏟️ Navy ground Monkey bay MH
📅 19 July 2026
🕛 2:30 pm
Nsanama young soccer vs Nselema united
🏟️ Vision stadium Ntaja
📅 26 July 2026
🕛 2:30 pm
Nsanama young soccer vs cobbe Baracks
🏟️ Vision stadium Ntaja
📅 1 August 2026
🕛 2:30 pm
Zomba Air base vs Nsanama young soccer
🏟️ Zomba Air base ground
📅 8 August 2026
🕛 2:30 pm
Nsanama young soccer vs prison united
🏟️ Vision stadium
📅 16 August 2026
🕛 2:30 pm
Chidziwiso kwama sapota onse oyikonda Team,
Nsanama young soccer Tinasankha kukasewelera pa Ntaja stadium pachifukwa chosaka thandizo la ndalama, monga tonse tikuziwila last season team itayamba kumene inangokunga ma games ochepa chabe pakhomo, koma Titaona ndi mene anthu amalowera Tinaona kuti zingofanana osakunga, ndie Ulendo uno Tasankha Ntaja Vision stadium ngati Home ground yathu
Tipepese pachifukwa ichi,
Komanso Tafuna team izolowere kumenyera koyenda ngati home ground chifukwa ikazapanga qualify kupita ku National Division league, home ground yathu izakhala ku Balaka monga mene a Ntaja united akupangila
Zikomo kwambiri