George fuu

George fuu Social life, simple

19/09/2025

voti yanga ine๐Ÿ™†โ€โ™‚๏ธ

23/08/2025
30/06/2025

Kuzizira kochimwitsa๐Ÿคฆโ€โ™‚๏ธ

01/10/2024

Vinako

30/09/2024

Komaso Zeze simungamupange compare ndi mwana okuti or pa JETU sanafike umenewo nde timati ugong'oli

Zeze Kingston kumalawi kuno ali mu level yayekha mu amapiano muja

Osamaphatikiza ana oti anakanunkha mkaka wamabere ndi Legend

28/09/2024

pano olo mkodzo wakhoma lakubafa woti mbuzi inyambite ukusowa ๐Ÿ˜‚ kwaipa ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ

Akamati chida chabambo amanena chimenechi
26/09/2024

Akamati chida chabambo amanena chimenechi

Basitu malinga ndikutenthaku Gee washevedwa kale
24/09/2024

Basitu malinga ndikutenthaku Gee washevedwa kale

24/09/2024

"Akuti mmandamo zukani mupange unfollow. Ma foni aikidwa pa office ya a DC."

Ma driver osathawira pa window ku school ya driving amachita kuziwiratu kuti this sign post imatanthauza ku mwayandikira...
23/09/2024

Ma driver osathawira pa window ku school ya driving amachita kuziwiratu kuti this sign post imatanthauza ku mwayandikira kufika pa msundwe osatulusa mutu pa window

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when George fuu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category