15/06/2020
Chidziwitso: tikufuna kulemba ntchito ma master ena ku sukulu yathu.Kwa amene mungakonde tipezeni ku inbox kwathu,koma mukhale kuti muli ndi blown belt kapena black belt..Mukozekeso kudzapanga spy tsiku ndipa 29 mwezi uno, ndalama yolembetsela ndi 1000.