18/08/2026
Nkhuku kuti zikule bwino komanso mwa nthanzi zimafunika kuzipatsa ma vitamins osiyanasiyana.
Ku Ziweto Agrovet Shops, tili ndi ma vitamins osiyanasiyana omwe m***a kupeleka ku Nkhuku zanu za lokolo, za nyama komanso za mazira. Mu video iyi alangizi athu akufotokoza zama vitamins omwe timapezeka nawo ku Ziweto Agrovet Shops.