Zochitika mziko

Zochitika mziko Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zochitika mziko, Sport & recreation, Lilongwe.

https://www.facebook.com/photo.php?fbid=561408146588721&set=a.140708981991975&type=3&mibextid=rS40aB7S9Ucbxw6v
27/11/2024

https://www.facebook.com/photo.php?fbid=561408146588721&set=a.140708981991975&type=3&mibextid=rS40aB7S9Ucbxw6v

Panopa ndiye nkhani imene Ili mkamwakamwa ndi yokhuzana ndi mankhwala awa.

Mankhwala amene amadziwika kuti ndi otalikitsa moyo, MA ARV.

Anthu ambiri atutumuka ndi uthenga womwe ukuzungulira mmasamba amchezo woti MA ARV asiya kupangidwa, ndipo ena akuti ma Company opanga mankhwala wa achita kulengezetsa pagulu kuti basi sapanganso ma ARV ena.

Kodi zimenezi ndi zoona? Nanga ndi zoona kuti ma ARV achotsedwa pa ndandanda ya mankhwala amene angatumizidwe ku mayiko ena monga kuno ku Malawi, Zambia ndi mayiko ena?

NKHANI YONSE IFOTOKOZEDWA BWINO LOMWE PABWALO PANO

Koma kunjaku kukuchitika zinthu ๐Ÿ˜‚
21/08/2023

Koma kunjaku kukuchitika zinthu ๐Ÿ˜‚

25/07/2023

Interpret the picture ๐Ÿคท๐Ÿผโ€โ™€๏ธ๐Ÿคท๐Ÿผโ€โ™€๏ธ๐Ÿคท๐Ÿผโ€โ™€๏ธ

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zochitika mziko posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share