15/11/2020
Part 2
Anord: wabwera iweyo Boba!!!
Mzake wina:Boba ,wangatu wakupondeleza English wakhoza 98% ,iweyo ndi second highest koma wakhoza 65%
Boba:ok ndakuvani
Anord: mmm apapatu km tisasiye kulimbikira
Boba:osaopa ,Mulungu sataya wake
Form 4 student's: apapatu ndiye wangatu watenga malo
Zaine:eee ndipo ,koma Bora asasiyire p***a
Class ya English inatha motelo ndipo ophunzira onse anayamba kupita makomo mwawo chifukwa period imeneyi inalinso yomaliza.weekend itatha ophunzira anabweleranso ku sukulu.
Wanga:Boba bhoo
Boba:bhoo
Wanga: zikuyenda?
Boba: eya Kaya iwe?
Wanga:inenso zikuyenda.Ndmakufunatu pa tea break k*ti tikambirane tinagwirizana zija
Boba: chabwino ndava
Wanga: unalemba Kare time table?
Boba: eya uyiwona titakumana
Wanga : ok
Nthawi ya break itakwana Boba ndi Wanga anakumana.
Wanga: time table yo ndiye ilibwino kwambiri
Boba:owoo
Wanga:iwe sukuwona?
Boba:mmm bas palibe chovuta chilichonse
Wanga:zoona
Boba:tikumanenso mawa bwanj chifukwa nthawi ya break ikuwoneka k*ti yathatu
Wanga: eya ndichoncho
Break itatha period yoyambilira analowa ndi aphunzitsi achichewa
Sir gamula: Kodi mneni ndichan.
Zaine:sir musanapitilize nanenso ndili ndi funso
Sir gamula: ok chabwino Funsa
Zaine:bwanj simupeleka Moni mukalowa mkalasi muno?
Sir gamula:aaaa Moni wachani Nanu ,ndimadziwa kale k*ti nonse mulibwino
Sir gamula anapitiliza kufunsa mafunso
Noria:mmeni ndi mawu amene amanena za ntchito yomwe ikuchitika,yachitika,idachitika kapena yomwe idzachitika
Sir gamula: wakhoza
Atangomaliza kuyankha funso noria anakumbukira za nkhani yomwe inkachitikachitika mu masukulu ambiri
Sir gamula: Kodi mawu oti kupondeleza amatanthauzanji?
Ophunzira onse anadabwa ndi funsolo ndipo ena anafuna kudziwa cholinga chomwe afunsira fusolo.
Anord:mmm sir mwafunsa funso limeneli chifukwa chani
Sir gamula: mesa ndine phunzitsi,ndkuyenera kufusa bas
Anord: owoo,nanga mu magawo a mmeni mulinso kupondeleza?
Part 2 yathera pano
Ndipitilize part 3??
Comment 💪💪💪💪