Esau Banda TK sports update

Esau Banda TK sports update updating sports in all sport activities this page its sports update only nothing else

12/06/2023

Be ready all mij sounds fans. Any time from now mij sounds bonanza is going to start to be confirmed date , venue and all requirements.

10/06/2023

Tikumbutsane kuti esau banda is back ndi nkhani zamasewero osiyanasiyana

20/06/2022

Zotsatira zamasewero ampira mu mij sounds bonanza ndi madera ena. Dzulo lamulungu thumbwi 1 m'bang'ombe rangers 0 pamene kwakayembe mpetsankhuli 1 mchalochalo 1 idzamenyedwaso. TNM noma 1 blue eagles 1. More to come tidikire felix kutikwasanthe ndi madera ena zatha bwanji. Zikomo keep on following.

14/06/2022

This coming weekend in mij sounds bonanza top 8 masewera ali pakati pa Nthumbwi fc eni bwalo vs m'bang'ombe rangers. Malo ndi pa chidalanda community center ground nthawi ndi 2:30pm. Bwerani nonse mudzaonerere kukoma kwa moira wa miyendo my mij sounds bonanza. Esau Banda ali konko kukupatsirani masewero amenewa live pa mij sounds. Mtengo pakhomo ndi 300

Send a message to learn more

30/05/2022

Mij sounds bonanza yafika mu top 8. Lamulungu likubwerari kuli chimwang'ombe hope vs chitukula fc. K300 mtengo 2:30 masewero akuyamba ,malo ndi pa chidalanda community center ground. Mij sounds ndikumtunda wawaaaaa .

Address

Esau Banda @ Kasungu TTC
Kasungu

Telephone

+265881817803

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Esau Banda TK sports update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category