MCLoud Zeka Sports Update

MCLoud Zeka Sports Update Doing Sports only

PETER MPONDA WAMUNG'ALULA CHIGOGAMalingana ndi Mphunzitsi wakale watimu ya FCB Nyasa Big Bullets Peter Mponda wati zinth...
04/08/2026

PETER MPONDA WAMUNG'ALULA CHIGOGA

Malingana ndi Mphunzitsi wakale watimu ya FCB Nyasa Big Bullets Peter Mponda wati zinthu zingapo zimaoneka ngati zikumuvuta ali k*timuyi chifukwa choti mkulu wa adindo k*timuyi Albert Chigoga sankamufuna k*timuyi in short anali galu ndi fisi.

Iye amayankhula pa pulogalamu ya Wa Ganyu Exclusive lachiwiri pomwe anali kufotokoza umoyo wake mu uphunzitsi.

Iye wati atapita ku Bullets, osewera ochuluka omwe ankadalilika anachoka komabe sanagulilidwe osewera omwe amawafuna.

"Tinapempha za Masiya Manda koma zinakanika kenako tinamvana ndi Chitipa United k*ti titenge Andrew Joseph koma zinakanidwa mpake tinayamba k*tenga osewera omwe alibe mgwirizano ndi timu iliyonse," anatero Mponda.

Iye wati kuchotsedwa kwake k*timuyi linali phuma kamba koti zina zomwe zinali mu mgwirizano wake sanaziyang'anire ndipotu kalata inamupeza ali mu bus.

Mponda wayankhulanso zokhudza Khuda Muyaba k*ti osewerayu ati sanakondwe ndi k*tulutsidwa pa masewero awo ndi Mighty Wanderers pomwe ankati iye si osewera otuluka pakati pa masewero.

Iye watinso timu yake ya Masters FC yaika mulingo wotenga ligi ya FDH Premiership kapena mu matimu anayi oyamba mu ligiyi.
kumpira ku eeee kuli ndale zoopsa

Ndipo lero Gangata anakumana ndi Khuda komaso osewera ena kuwauza zoti azinvera coach ndipo ngt yemwe sakufuna timui achoke ndipo Khuda anavomera k*ti achoka ndipo Gangata wamuuza k*ti abweze K10million yake ya signing on Fee yomwe Khuda anapochela
awa akufunika ku mental iyiyi ndimisala

Khuda Ikelembe Muyaba who signed with Masters Security Football Club has accepted to part with the team mutually agreed ...
04/08/2026

Khuda Ikelembe Muyaba who signed with Masters Security Football Club has accepted to part with the team mutually agreed after Misunderstanding with his coach Peter Mjojo Mponda
Gangata met with Khuda today to discuss about the issues ndipo Gangata anamuuza Khuda k*t aliyese azivera Coach chifukwa timuyi amamupatsa coach kt azitsogolera ndipo amene sakufunako k*timui achoke of which Khuda accepted k*t he want to leave.
ndipo Gangata wamuuza k*t abweze ndalama zokwana K10million za Signing on Fee ndipo Khuda wavomera
Kodi amenei vuto lake nchan koma??? munthu otemberereka km

HEAD-TO-HEAD: Malawi 🇲🇼 vs Zambia 🇿🇲 (Women's National Teams)The rivalry between Malawi and Zambia has grown into one of...
03/08/2026

HEAD-TO-HEAD: Malawi 🇲🇼 vs Zambia 🇿🇲 (Women's National Teams)

The rivalry between Malawi and Zambia has grown into one of Southern Africa's most competitive women's football matchups. As the two neighbours prepare to face each other again on Tuesday, history suggests fans should expect another entertaining contest.

Previous Meetings:
2025: Malawi 1-1 Zambia
2025: Zambia 2-3 Malawi
2025: Zambia 2-0 Malawi
2024: Malawi 0-2 Zambia
2023: Zambia 1-2 Malawi
2021: Zambia 3-2 Malawi
2021: Malawi 1-1 Zambia
2020: Zambia 0-1 Malawi
2012: Malawi 4-2 Zambia

Recent H2H Record (9 Matches):
🇿🇲 Zambia Wins: 3
🇲🇼 Malawi Wins: 4
🤝 Draws: 2

With both sides enjoying victories over each other in recent years, this fixture has become one of the most unpredictable in the region. Zambia will be aiming to level the historical record, while Malawi will look to continue their impressive run against the Copper Queens.
Who do you think will claim all three points on Tuesday?





Apa ndi 50:50

Timu ya TN Stars ya m'boma la Kasungu yalemba ntchito Meck Mwase kukhala m'modzi mwa aphunzitsi ake.Mlembi wamkulu wa ti...
22/06/2026

Timu ya TN Stars ya m'boma la Kasungu yalemba ntchito Meck Mwase kukhala m'modzi mwa aphunzitsi ake.

Mlembi wamkulu wa timuyi a Symon Mataka wati Mwase yemwe anakhalapo mphunzitsi wa timu yampira wamiyendo ya fuko lino komanso Mighty Wanderers wayamba kale ntchito yokonzekeretsa anyamata a Ngulanawambe.

Mwase agwila ntchito ngati Technical Director wa timuyi, udindo omwe aziona m'mene aphunzitsi amnzake akugwilira ntchito yosula osewera.

Mwase yemwe adaphunzitsakonso timu ya Nsingizini Hotspurs ya m'dziko la E-Swatini watsimikiza za kufika kwake ku timuyi ndipo agwila ntchito ndi Limbani Mwakhwawa amene ndi m'phunzitsi wa mkulu wa timuyi pakadali pano.

Lamulungu likudzali TN Stars isewera ndi Manzochiso pa masewero otsekulira mpikisano wa ligi ya chigawo cha pakati pa bwalo la Kasungu.

Mwase ndi yemwe adayitsogolera TN Stars kulowa mu ligi yayikulu ya m'dziko muno yomwe imatchedwa k*ti TNM Super League pa nthawiyo.

THEMBA ZWANE MAKES WORLD CUP HISTORY FOR ALL THE WRONG REASONS🇿🇦Football fans have seen some quick goals, dramatic subst...
12/06/2026

THEMBA ZWANE MAKES WORLD CUP HISTORY FOR ALL THE WRONG REASONS🇿🇦

Football fans have seen some quick goals, dramatic substitutions and unforgettable moments over the years, but Themba Zwane may have just set one of the most bizarre records in South African football history.

The Bafana Bafana veteran was shown a red card just 3 minutes after coming onto the pitch during South Africa’s FIFA World Cup campaign, turning what should have been a routine appearance into a moment that fans will be talking about for years. 😳🟥

Zwane has built a reputation throughout his career as one of South Africa’s most gifted and respected footballers. That’s why many supporters were left stunned when his World Cup appearance ended almost as quickly as it began. One moment he was entering the game, and before fans could settle into watching him play, the referee was already reaching for the red card.

Football can be cruel sometimes. Players dream their entire lives of stepping onto the World Cup stage, but very few expect their tournament moment to last only 3 minutes. Despite the unfortunate record, Zwane remains a Bafana Bafana legend whose contribution to South African football goes far beyond one incident. 🇿🇦⚽

Will this go down as the most unfortunate World Cup cameo in South African football history? 🤔💯

very very bad to SA tingot next time muzepulako anu nanu

FIFA WORLD CUP OPENING MATCH FULL TIME Mexico 2-0 South Africa
11/06/2026

FIFA WORLD CUP OPENING MATCH

FULL TIME

Mexico 2-0 South Africa

Crerk Sporting Club Pated way with there coach Elia Guadiola Kananji plus assistant coach more ine the photo below
10/06/2026

Crerk Sporting Club Pated way with there coach Elia Guadiola Kananji plus assistant coach more ine the photo below

It's Officially Wedson Nyirenda AKA Wadada has joined FCB Nyasa big bullets for this year 2026 campaign mwamulandira bwa...
10/06/2026

It's Officially

Wedson Nyirenda AKA Wadada has joined FCB Nyasa big bullets for this year 2026 campaign

mwamulandira bwanji maule amenei kod nde mpulumutsi uja???

NEWS UPDATE.....FCB Nyasa Big Bullets yati ikufuna kulembera Super League of Malawi (Sulom) pofuna kuwadziwitsa k*ti mas...
10/06/2026

NEWS UPDATE.....

FCB Nyasa Big Bullets yati ikufuna kulembera Super League of Malawi (Sulom) pofuna kuwadziwitsa k*ti masewero awo apakhomo azigwiritsa bwalo la Mpira mu nzinda wa Blantyre osati Joyce Chitsulo ku Mwanza ngati m'mene zinaliri.

Mkulu oyendetsa ntchito zatimuyi, Albert Chigoga, wati chiganizochi chabwera pofuna kupereka mpata kwa ochemerera awo ozungulira mu nzinda wa Blantyre k*ti azitha kuonera masewero.

Chigoga watinso akuchoka pa bwalo la Joyce Chitsulo kamba koti osewera likuwavuta potengera k*ti sachitirapo zokonzekera.

Pamasewero atatu omwe Bullets yagwiritsa ntchito pabwaloli, yakwanitsa k*tolera mapointi asanu pamapointi asanu ndi anayi omwe amayenera kupata akanakhala k*ti anapambana.

Mapale anafanana mphamvu ndi Moyale FC 1-1 komanso Red Lions posagoletsana chigoli chili chonse, ndiponso anagonjetsa Mafco FC ndi chigoli chimodzi kwa duu mumasewero a FDH Bank Premiership.

Your Flames XI to face Ethiopia in Dire Dawa.
09/06/2026

Your Flames XI to face Ethiopia in Dire Dawa.

Address

Kasungu

Telephone

+265991065182

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MCLoud Zeka Sports Update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to MCLoud Zeka Sports Update:

Shortcuts

Share

Category