Nyasa Bullets vs Beforward Wanderes

Nyasa Bullets vs Beforward Wanderes Wanderers fc vs Nyasa Bullets

22/07/2026
22/07/2026

Amene akufuna timpatse u Admn hit inbox

22/07/2026

Football ⚽

01/02/2026

📌Hammers vs Wanderers
56
Khaa'
Issac Kaliati scores from the spot
Mzuzu City Hammers 0-1 Mighty Wanderers

240 games. 38 referees. Check out the 2025 TNM Super League
08/01/2026

240 games. 38 referees. Check out the 2025 TNM Super League

WOSEWERA MPIRA WA TIMU YA ALGERIA MOHAMED AMOURA WAPEPETSA Mohamed Amoura wapepetsa kwa ochemelera wa timu ya dziko la D...
08/01/2026

WOSEWERA MPIRA WA TIMU YA ALGERIA MOHAMED AMOURA WAPEPETSA

Mohamed Amoura wapepetsa kwa ochemelera wa timu ya dziko la D.R Congo pomwe anayerekezera momwe ochemelera wa timu ya Congo amapanga poimilira, osegwedela ndikuimika dzanja m'mwamba pa masewero onse a timu ya Congo ndipo izi zimaimila, Patrice Lumumba chizindikiro chosonyeza kuziimila paokha kwa dziko la DRC, kuchoka muokapolo, kukhala ozilamulira okha.

M'mawu ake Amoura wati masewero omwe amasewera ndi Congo anali masewero akulu, opatsa ntheng'eneng'e m'bwalo lazamasewero.

Ndikufuna anthu andimvetsetse panthawi yomwe ndimayesezera Lumumba sindimaziwa zomwe zimatanthauza, ndinangopanga mwansangulutso chabe ndinalibe lingaliro lilironse lonyoza kapena kufuna kuyambitsa kusamvana.

Ndimalemekeza timu ya Congo ndipo ndikuifunira zabwino zonse pomwe ikukapikitsana nawo pa masewero ofuna kuzigulira malo ku mpikisano wa pa dziko lonse omwe uchitikire ku maiko a America, Mexico ndi Canada.

Ngati kachitidwe kanga kanali kosokoneza ndikupepetsa chifukwa sichinali chikonzero changa.

Timu ya Algeria inagonjetsa D.R Congo ndichigoli chimodzi kwa duu chomwe chinabwera mu mphindi 90 ndi 29 zowonjedzera mwapadeladela.

08/01/2026

Kung’unde Chooses Bullets Over Silver Strikers.

Deal Done✔️

Bullets have completed the signing of defender Ahmad Kung’unde, beating competition from Silver Strikers to secure his services.

The 24-year-old centre-back has been without a club since his contract with Mighty Wanderers officially ended on 16 September 2025. Kung’unde was sidelined during the entire second round of the season at Wanderers due to circumstances that limited his involvement with the team.

Sources close to the deal have confirmed that all agreements are now in place. Kung’unde has signed a three-year contract with Bullets, which will officially commence on 1 March 2026.

Bullets have already paid a K8.6 million signing-on fee, with the club now awaiting final clearance after settling outstanding payments to Chitiyo, expected to be completed this week. Once the February transfer window opens, Bullets are set to officially announce the signing of Kung’unde, along with other new recruits.

The move marks a fresh start for the talented defender as Bullets continue to strengthen their squad ahead of the new season.

08/01/2026

🤯 One day was enough to turn expectations upside down in the Premier League.

The fall continues for the big teams… no safety on Matchday 21! ❌

⚪️ Tottenham fall to Bournemouth
🔵 Chelsea lose to Fulham
🔵 Manchester City stumble against Brighton
🔴 United settle for a point against Burnley

Address

Dwangwa

Telephone

+265881648701

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyasa Bullets vs Beforward Wanderes posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category