Scotch at Soccer Show.

Scotch at Soccer Show. The Winning Zone. ⚽πŸ”₯

01/09/2026

Follow
LiteraConsult Research Solutions

  For more information follow LiteraConsult Research Solutions
01/09/2026



For more information follow
LiteraConsult Research Solutions

01/09/2026
PETER FOTE>CHOMWE CHABAYA BOB MPINGANJIRA NDI TADIKILANI KAYE:Sanudi  ndi Gard Chirwa  kumuuza coach  kuti mbali iyo sii...
01/09/2026

PETER FOTE>CHOMWE CHABAYA BOB MPINGANJIRA NDI TADIKILANI KAYE:

Sanudi ndi Gard Chirwa kumuuza coach kuti mbali iyo siili bwino tithandizeni musinthe kuyankha kwa Bob amangoti tadikilani kaye.

Azake a technical kumuuza Bob mbali iyo ikufunika kusintha kuyankha kwa coach Bob amati tadikilani kaye.

Peter 40 watelo kuti TADIKILANI KAYE wapwetekesa Bob.

Parry Chinyama > Ugonthi wapwetekesa Bob kosafuna kuva zazake ndipo amene uja sabwelelaso ku Malawi kuno timu ikakuyimisa ndi zovuta kuti ubwelele.

Innocent Mphongolo > Timu ya Mighty Wanderers izandikila mochedwa kuti Bob sanayenera kupasa contract koma amasowa pomuyimisila apa apeza chifukwa pomwe aluza ndi Ekhaya Fc. Bob Mpinganjira League yakulila iye uja akuyenera reserve ndikomwe amachita.

Inu maganizo anu ndi otani akutitu uyu sabwelaso ku timu oyimisidwa omwewo azalandila kalata yochoseledwa ali kukhomo.

Pangani follow Wa Mpira Sakwiya kuti muthe kumalandila nkhani zabwino zabwino pano.

01/09/2026
Zatsimikizika sopano kuti timu ya Mighty Wanderers yasankha mphunzisi wakale wa timu ya dziko lino Patrick Mabedi ngati ...
01/09/2026

Zatsimikizika sopano kuti timu ya Mighty Wanderers yasankha mphunzisi wakale wa timu ya dziko lino Patrick Mabedi ngati mlangizi wamkulu wa timuyi (Technical Director)

Malingana ndi zomwe tapeza McDonald Mtetemera ndiye wasankhidwa kukhara mphunzisi oyembekezera wa timuyi kusatira kuchotsedwa Kwa Mphunzisi wamkulu Bob Mpinganjira.

Timu ya Mighty Wanderers FC yachotsa mphunzisi wamkulu wa timuyi kusatira kugonja ndi timu ya Ekhaya FC mpikisano wa Airtel Top 8 pa bwalo la Bingu Stadium

31/08/2026

Mukuti wapachibale umenewu πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Mphunzitsi wa might wanderers Bob mpinganjira wasankhidwa ndi Bungwe la football association of Malawi kuti aphunzitsi t...
31/08/2026

Mphunzitsi wa might wanderers Bob mpinganjira wasankhidwa ndi Bungwe la football association of Malawi kuti aphunzitsi timu ya Malawi under 23 yomwe isewele ndi ESWATINI mu Africa cup under 23 ndipo opambana azasewela ndi Algeria

Address

Dowa

Telephone

+265882952904

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Scotch at Soccer Show. posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Scotch at Soccer Show.:

Shortcuts

Share