Sêñïør³

Sêñïør³ Latest vacancy

december💔
05/12/2025

december💔

20/11/2025
20/11/2025

It is well ♥️

20/11/2025
Tima Harmonize ting'onoting'ono..🙌🙌🙌 I think ndipangitse show uyuyu akhalepo ndizangowauza anthu kuti ndaitana Harmonize...
20/11/2025

Tima Harmonize ting'onoting'ono..🙌🙌🙌

I think ndipangitse show uyuyu akhalepo ndizangowauza anthu kuti ndaitana Harmonize Kubangwe! ..🔥🔥

Anyways go and subscribe he's YouTube account!
Watulutsa Nyimbo ndendende Harmonize yo ..

Dzina lake ndi Fredoniah
M***a kumuitanaso kuti Fredonaize mutafuna .😂

Here is the link .

https://youtu.be/gXo22QgnuoQ?si=KrzBTsS5ZB3ROCr0

kutseka chaka
20/11/2025

kutseka chaka

Zolengeza ndi izi

20/11/2025


Apolisi atsimikiza za kumangidwa kwa m'modzi mwa anthu odziwika bwino ndi nkhani yojambula nyimbo komanso pa masamba a mchezo VJ Ken.

Malingana ndi mneneri wa polisi ya Ndirande a Chibisa Mulimbika, ati VJ Ken yemwe dzina lake ndi Kenneth Makina wa zaka 30, watengedwa pomuganizira kuti amasunga msungwana wa zaka 15 mokakamiza.

A Mulimbika ati mwanayu yemwe wakhala akusowa kuyambira pa 15 November, wapezeka dzulo ndipo wawululula kuti wakhala ali kwa VJ Ken yemwe ndi bwenzi lake.

Apolisi ati mwanayu wawululanso kuti wakhala ali pa ubwenzi ogonana ndi VJ Ken.

(by Innocent Kumchedwa -Lilongwe:11/19/25)

20/11/2025

Woman Crush Wednesday, Ritaa 🔥

Nyimbo Ikhale YOCHOKELA MU Kachikena Album,

20/11/2025

Wikise1992 ndi Miracle Vic Chinga , anakomenta pa Tiktok pomwe ndayika clip ya imodzi mwa Nyimbo Zimene Zili MU album ya Kachikena, zikuoneka kuti anzangawa zawa kondweletsa.

Ndipo makomenti Awo andilimbikitsa heavy 🔥

Stream My New Album Kachikena Here 🔥👇
https://open.spotify.com/album/6PENsKHjn2r8Zmg9dIBvQ4

20/11/2025

Ambuye dalitsani amene tadzuka kalefe enawa ndima rich kids siakugona??
Good morning bwezi 🤭

Address

Chimamba, Linthipe 1
Dedza
KÀPPÀ39

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sêñïør³ posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Sêñïør³:

Share