01/08/2023
Olo titafa bola second Quarter tawina 15-12, adziwanso kuti Takondwa Lwazi uja anangofupika koma ndi Micium Mhone pa yekha.
Joyce Mvula ndi Christopher Kumwembe ndipo Mwawi Kumwenda ndi Gabadinho Mhango. Grace Mwafulirwa ndi Francisco Madinga, Thandie Galeta ndi Yamikani Chester. Panjapo palitu Peter Banda Jane Chimaliro.