Za Mpira

Za Mpira Football news from Malawi 🇲🇼 and around the World🌍🗺️⚽🔥🎯 daily updates 🔥

03/09/2026

With Za Mpira – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

Breaking news: Here we go💣💥Christopher Kumwembe wasayina pre contract NDI Bullets deal ya 2 Years🎯Zonse zatheka ndipo an...
03/09/2026

Breaking news: Here we go💣💥

Christopher Kumwembe wasayina pre contract NDI Bullets deal ya 2 Years🎯

Zonse zatheka ndipo angodikira kuti miyezi yochepa ikubwerayi contract yake ndi Manoma ithe ndipo ayambe kukankha chikopa ku Maule⚽

Osaiwala kupanga follow kuti nkhani zamasewero zisakuphonyeni💪

02/09/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Fred Moya, Esau Sefu, Offical Tata Chiwaya, Tonny Chagundah Jnr, Unique Bester Seleman, Haward Gama, Kumbukani Kumtso KT Kadewere, David Misamo, Mike Banda, Sallyz Wamanoma Makampan, Peace Edward, Bernard Bwanali, Humphlys Kalex, Justin Matiya Chipembere, Shelis Alex Chiwaya, Mwenimulesu Mulesu, Patrick Chagaka, Mphatso Lewis Mwenyemas, Alfred Haneck Kantuwanje, Meadson Ngala, John Zadyera, Fadhili Kondo, Biliat Storo, Chisomo Shumba, Ernest Martin, Takalani January, Loyd Limbani, Zexy Cronex Wawala, Achirenje FatoSousa Nbf, Mazon J Phodo, Ntambo Alfazema, Star S Aims Phungu, Davis Beulah, Louis Makwinja, Davie Kaponda, Vengelical Capten Kasuzi, Lovemore Kankhadze, Damiao Santos Domingos Domingos, Stivie Lambulira, Ntopa Philip, Mario Gabriel Isaac, George Sinjela, Richard Chibisa, Hangry Lingison, Andy Samson, Oscar Vicker, Mphatso Wa Salo Amos, Adack Sahad, Coster Masame, Precious Nachiye

 Timu ya Mighty Wanderers Fc yawonesa chidwi chofuna kutenga mphunzitsi wakale wa timu ya Malawi Patrick Mabedi komanso ...
31/08/2026



Timu ya Mighty Wanderers Fc yawonesa chidwi chofuna kutenga mphunzitsi wakale wa timu ya Malawi Patrick Mabedi komanso yemwe akuphunzitsa timu ya Master FC, Peter Mponda.

Wanderers Fc yalengeza utsiku wapitawu kuti yamuyimisa mphunzitsi wawo wamkulu Bob Mpinganjira, kamba kosachita bwino mumpikisano wa Airtel Top 8 pomwe yagonja dzuro ndi timu ya Ekhaya FC.

Padakali pano akulu akulu a Mighty Wanderers Fc afikira aphunzitsi awiriwa omwe akuchita nawo zokambirana.

Wanderers ikuyembekezeka kukumana ndi timu ya Simba SC yaku Tanzania mumpikisano wa CAF Champions League Lamulungu likuzali pa 6 September 2026 pa bwalo lazamasewero la Bingu munzinda wa Lilongwe.

Zambiri zikuchitika pangani follow kuti zonse zisamakuphonyeni⚽⚽

kodi mukudziwa?Anzanutu akupanga ndalama pongotsewera game 🎮 pa phone yawo ya m'manja.Chomwe mungachite mungopanga downl...
31/08/2026

kodi mukudziwa?

Anzanutu akupanga ndalama pongotsewera game 🎮 pa phone yawo ya m'manja.

Chomwe mungachite mungopanga download the app kugwiritsa ntchito link ili mmutsiyi.

https://playbb.fun/u/31118675.

Earn more points with a single purchase, enjoy smooth dragging and intelligent attachment. Invite friends to unlock revival opportunities.

Umu ndi mmene Mighty Wanderers yayambira masana a tsiku la lero.16. Dalitso Khungwa12. Stanley Sanudi22. Emmanuel Nyiren...
30/08/2026

Umu ndi mmene Mighty Wanderers yayambira masana a tsiku la lero.

16. Dalitso Khungwa

12. Stanley Sanudi
22. Emmanuel Nyirenda (C)
13. Timothy Silwimba

25. Felix Zulu
8. Blessings Singini

11. Mphatso Kamanga
10. Gaddie Chirwa
33. Dalitso Nahipa

30. Clement Nyondo
7. Sama Thierry Tanjong

Osaiwala kupanga follow kuti mutsatire bwino wasewera amenewa⚽

💥 💥 💣💣Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yalengeza kuti yasaina katswiri womwetsa zigoli wamdziko la Zimbabwe Tinaye Tsimba k...
27/08/2026

💥 💥 💣💣

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yalengeza kuti yasaina katswiri womwetsa zigoli wamdziko la Zimbabwe Tinaye Tsimba kukhala wosewera wachiwiri kumusaina pa msika wogula ndi kugulitsa osewera.

Tsimba yemwe ali ndi zaka 23 zakubadwa wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi ndipo akhale akuoneka kutimuyi tsopano.

Osaiwala kupanga follow for more transfer updates 💣⚽

Mutakhala Kochi wa Malawi the Flames ndipo muli ndi akatswiri osewera pakati (Defending Midfielders) Atatu koma MUKUFUNA...
27/08/2026

Mutakhala Kochi wa Malawi the Flames ndipo muli ndi akatswiri osewera pakati (Defending Midfielders) Atatu koma MUKUFUNA kuyambitsa game mmodzi, wina pa benchi wina mungomtaya palipose!

🟡Lloyd Njaliwa
🟡Aaron Banega Lloyd
🟡Yankho Singo

Mukhoza kupanga motani kuti game muwine?

Osaiwala kupanga follow ⚽

26/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chimzy Sungani, Chidakwa Levison Lackson Tomas, Fatuma Best Smooth, Chisomo Kaonga, Kodwani Mauden, Lenadi Nkhoma, Rundu WA Medson Temboh, Blessings Bandah, Yahaya Said, Gift Boy, Josephy Pindan Dilon, Austin Wasopano Sapangwa, Joseph Charles, Andrew Ky Kamnkhwani, Lateefah Hassan, Yohane Wyson Kachingwe, Adams Damzy Kapetuka, Yasoni Nkhoma, Kanyamalibw Ellijah, Ruben Phiri, Thomas kamenya, Keneth C Kadura, Josey MJ Mady, Feristar Kutsanda, Lucas Mangala, Gomezha Mbaly, James Jesnao, Jumullah Jamesd, Buba Mdoka, Wang Xing Chang Feng, Omar Matola, Dingi Gift Luhangas, Malata Precious, Alex Petet, Kanyenda Lucious, Anemwe Ødekha Abalizø, Collings Msenga, Aubameyang Asufant, Bliss Jackson, Vistone Malilo, Lloydmw Namalamba, Chauncy Mlambuzi, Harrison AK Chitsamba, Yesaya Nkoma, Chikafa Leonard, Edward Halla, Fletcher Chande, Gift M Ntanga, Jane Zaipa, Benson Maseko

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Za Mpira posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share