Sports Agenda Malawi

Sports Agenda Malawi To discuss all the issues concerning sports updates and info of local sports and international.

Zathela mofananitsa Mphamvu
06/06/2026

Zathela mofananitsa Mphamvu

MPHATSO SITIMADELELABungwe loyendetsa Mpira kuno ku mudzi la FAM lalandila mipila yogwilitsidwa kale ntchito (second han...
05/06/2026

MPHATSO SITIMADELELA

Bungwe loyendetsa Mpira kuno ku mudzi la FAM lalandila mipila yogwilitsidwa kale ntchito (second hand balls) yokwana 36 Kuchokela ku Japan Football Association

Izi zithandizila kuti ubale pakati pa maiko awili wa ukule komaso tizithandizana muzambiri

Ma Club enawa atangoti azichepesa kuchilemba ntchito ichichi Ma Timu anuwa adzukatuEven upangili okha akhoza kukupasanit...
02/06/2026

Ma Club enawa atangoti azichepesa kuchilemba ntchito ichichi Ma Timu anuwa adzukatu

Even upangili okha akhoza kukupasanitu

2026 season Mpira wayaka

01/06/2026

Uthenga sulemela ndipo umveke muliko

30/05/2026

Aaah Za satanic zo

Timu ya Ndirande Stars yalowa mu Mgwilizano ndi kampani ya Sharma Electrical leroIwowa apaleka uniform za ndalama yokwan...
18/05/2026

Timu ya Ndirande Stars yalowa mu Mgwilizano ndi kampani ya Sharma Electrical lero

Iwowa apaleka uniform za ndalama yokwana 15 million kwacha ndipo ati pakadutsa miyezi isanu ndi umodzi agula bus yoti timuyi izigwilitsa ntchito

Nathan Sharma kuchokela ku Kampaniyi wati malingalilo otengelatu timuyi kukhala yawo alipo ndipo zonse akukambilana ndi amtsogori a Ndirande Stars

Ndirande Stars ikusewera mu mipikisano wa NBS National Division League pomwe masewero awo oyamba afananitsa mphamvu ndi FOMO FC pa bwalo la Mulanje

It's too earlyMa coach athotholedwa season ino
18/05/2026

It's too early

Ma coach athotholedwa season ino

Final results ya National Division LeagueMa Timu atolela ma points motere
17/05/2026

Final results ya National Division League

Ma Timu atolela ma points motere

Chi League cha Nyatwa ichiWeekend imeneyo maswero alipo motere, ulendo otaya ndi kutolela ma points mu NDL wayambikaAdut...
14/05/2026

Chi League cha Nyatwa ichi

Weekend imeneyo maswero alipo motere, ulendo otaya ndi kutolela ma points mu NDL wayambika

Adutse ndani apa

😜 My fellow football loversMalingana ndi mmene zakhalila ndi west ham, ife timati tilengeze kuti chinthuchi chapita basi...
10/05/2026

😜 My fellow football lovers

Malingana ndi mmene zakhalila ndi west ham, ife timati tilengeze kuti chinthuchi chapita basi moti atsogola kwambili moti sangapezekenso

Ndi mau amenewa tiyeni tiwafunile zabwino ma gunners

Address

Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sports Agenda Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Sports Agenda Malawi:

Share