Gift Martial Wanya

Gift Martial Wanya Never give up

01/06/2024

Ngati week inoyo siziyamba kundiyendela πŸ™Œ ndiziyendera ndineyoπŸ™ŒπŸ˜‚

28/05/2024

Ujayi mati amabwela yekha uja 🀦,lero wabwela ndi akwawo 🀣🀣🀣
🎢🎢🎢

27/05/2024

A goal without a plan is just a wish
Good morning πŸŒ…

26/05/2024

Hello πŸ‘‹

15/05/2023

Pena pake pakayenda bwino .... Nditukwana wina wake 😲
Iwe!! Konyera kuno!!?

08/05/2023

Pano nasiya kukakamiza zinthu .....or Ma units akakana kulowa kamodzi komweko πŸ“± ndimataya.......πŸ«‚πŸš«

03/05/2023

Kadzi azikhala modzi mwamva ...... Zambiri zizikhala ndalama πŸ’ΈπŸ’Έ

Team mwayiphula mesa πŸš—πŸ’₯🐲

17/02/2023

mutipeze ife tikuthandizeni.....

wawelenga kuyimva momwemo....... ndili free anytime 😊 mundipeza.....

19/01/2023

ineyo ndi Bwana ....... Koma inuyo simadziwa.........

Cool kumvera sound 🎡🎧

13/01/2023

Koma ndachoka kutali.....
Mulungu anali plan.....

29/08/2022

Mojo released by Driemo. This RnB song is now available for download from malawi-music.com to your phone or computer.

Address

Nazombe Ghetto
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Gift Martial Wanya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Gift Martial Wanya:

Share

Category