Malawi Football Lovers PAGE

Malawi Football Lovers PAGE Simply known by MFLP, is a fast-growing Malawian platform for local and international sports updates. We'll be providing loads of exclusive such us autographs.
(2)

The Malawi Football page aims to keep you tight up to date with Malawi football. We'll also be releasing news on the monthly TNM SUPER LEAGUE PLAYER OF THE MONTH AND MANAGER here as soon as it is announce. And you'll be able to get involved in the voting process as a fan. We're keen to hear your feedback on what we're doing with the Page. Please note that this is a friendly forum and while we wan

t you to send your views, we reserve the right to remove any posts that could viewd as obsecene. Defamatory,abusive or threatening to thers, promotiobal messages are disallowed and will be removed. Failure to comply with these rules may result in us reporting and blocking offenders. (www.mflp.com)

12/06/2026

"The World Cup is also telling Neba to go beck home." Anthu M'magroup.

Bungwe la FIFA layika malamulo atsopano onena kuti matimu asiye zomamutenga osewera wa timu yaikulu kumupititsa ku timu ...
12/06/2026

Bungwe la FIFA layika malamulo atsopano onena kuti matimu asiye zomamutenga osewera wa timu yaikulu kumupititsa ku timu yawo yaing'ono kapena kuti azipanga zokonzekera payekha ngati njira yopereka chilango kapena yomuthamangitsira ku timu imeneyo.

A FIFA ati osewera akhala akuzunzika ndi zinthu ngati izi kwa nthawi yaitali ndipo kuphwanyira ufulu osewera mu njira iyi kutheretu. Timu yomwe izipezeka ikuphwanya lamulo limeneli pazikhala chilango chachikulu kwambiri.

Bungweli latinso, kwa matimu omwe amakhalitsa osalipira osewera awo. Nthawi yoti awalipile ikadutsa, ndalama zija ziziyamba kukwera ngati katapila wa 8% (will incur 8% interest rate). Ndiye ngati pali matimu omwe amatha nthawi osalipira osewera awo, nthawi yowalipila ikakwana, pazikhalapo koonjezera kenakake malingana ndi momwe malamulo amenewa anenera.

12/06/2026

Ambiri tikugona 🛌

FULL TIME
South Korea 2-1 Czech Republic

11/06/2026

Game over

World Cup yayamba mwa drama ma red card mpaka atatu, awiri ku SA imodzi ku Mexico.

Mexico 2-0 South Africa

11/06/2026

Zwane red card atamumenya mbama osewela wa Mexico zadala.

Madzi akupitilira kuchita katondo ku SA

Ma red card awiri tsopano.

87 minutes zatha still 2-0

11/06/2026

MPHWAAAAAAAA!!! Mexico again

Raul Jimenez

Mexico 2-0 SA

68 minutes..

And SA yalandira red card....

11/06/2026

Half Time

Mexico 1-0 SA

11/06/2026

HYDRATION BREAK OVER, PLAY RESUMES

31' MEXICO 1-0 SOUTH AFRICA

11/06/2026

3 MINUTES OF HYDRATION BREAK,

26' MEXICO 1-0 SOUTH AFRICA

11/06/2026

Gutierrez of Mexico also yellow carded for a bad tackle on Mokoena.

24' MEXICO 1-0 SOUTH AFRICA

Address

Commercial Road
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Football Lovers PAGE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Football Lovers PAGE:

Share