Chaka Cha Mayakho ku Manoma

Chaka Cha Mayakho ku Manoma Sports

Mighty Wanderers week 7 play of the week its congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 wapata K300pin kuchoka ku kingbossi motorcycle.
17/06/2026

Mighty Wanderers week 7 play of the week its
congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉 wapata K300pin kuchoka ku kingbossi motorcycle.

Mongukumbutsana sabata ino ndi ya FDH Bank Premiership ndipo masewero alipo loweruka pa 20 June 2026 pa Mpira/Chiwembe s...
16/06/2026

Mongukumbutsana sabata ino ndi ya FDH Bank Premiership ndipo masewero alipo loweruka pa 20 June 2026 pa Mpira/Chiwembe stadium kuyambila nthawi ya 2:30pm.Mighty Wanderers against Ekhaya Fc,monga noma ili pa nkhomo umu ndimene mitengo ya pa gate iliri;
Open stand K10pin
Covered/vip K20pin.

FDH Bank Premiership






💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

Fdh Bank premiership yabweranso mu week 7 itapumilidwa Kwa sabata ziwiri kamba ka friendly ya flames ku Ethiopia komanso...
15/06/2026

Fdh Bank premiership yabweranso mu week 7 itapumilidwa Kwa sabata ziwiri kamba ka friendly ya flames ku Ethiopia komanso chinkho cha Airtel top 8.Msabataya nambala 7 wanderers ili pa nkhomo pa chiwembe/mpira stadium pomwe ikhale ikukumana ndi Ekhaya fc kuyambila 2:30pm.Tinakali pa number 1 ndi masewero 7 mapoints 12.








💙

King Boss player of the week 7 nominations are out.The winners will receive K300pin cash.Competitors are three players n...
15/06/2026

King Boss player of the week 7 nominations are out.The winners will receive K300pin cash.
Competitors are three players namely
1.Blessings Mwalilino
2.Felix Zulu
3.Dalitso Khungwa

Whom do you vote for???





.
💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙

At home ??  kunjoya Scottish football ⚽⚽ potsatila Scottish philosophy pamsi pa black Scottish coach  Mtetemera.Kupamban...
14/06/2026

At home ?? kunjoya Scottish football ⚽⚽ potsatila Scottish philosophy pamsi pa black Scottish coach
Mtetemera.Kupambana game yoyamba pa khomo next tikupita kwawoko kwa Creck komko.






Game over Mighty Wanderers 2-0 Creck Sporting Blessings Mwalilino 47'Lameck Mithi 49'@ mpira stadium  ndiyemwe wasakhidw...
14/06/2026

Game over
Mighty Wanderers 2-0 Creck Sporting
Blessings Mwalilino 47'
Lameck Mithi 49'
@ mpira stadium

ndiyemwe wasakhidwa kukhala osewera yemwe wasewera bwino kuposa anzake pa game imeneyi.
Congratulations 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
.

14/06/2026

90+3added
still
Noma 2-0 creck

Substitute Adam,Kamanga,kudonto and swilimba in.....Nahipa,Singini,Kaliati and NyirendaoutstillNoma 2-0 Creck
14/06/2026

Substitute
Adam,Kamanga,kudonto and swilimba in.....

Nahipa,Singini,Kaliati and Nyirenda
out

still
Noma 2-0 Creck

75minutes stillNoma 2-0 Crecknthawi nde ikusendera apa wezwez
14/06/2026

75minutes
still
Noma 2-0 Creck
nthawi nde ikusendera apa wezwez

Kubwera wave after wave manoma kufunabe zigoli Zina kuti iduliretu khosi stillNoma 2-0 Creck mwalilino 47'mithi 49'
14/06/2026

Kubwera wave after wave manoma kufunabe zigoli Zina kuti iduliretu khosi
still
Noma 2-0 Creck
mwalilino 47'
mithi 49'

Address

Lalilubani
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chaka Cha Mayakho ku Manoma posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chaka Cha Mayakho ku Manoma:

Share

Category