Za masewelo Mchichewa

Za masewelo Mchichewa Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Za masewelo Mchichewa, Sports, mondiwadalitso@gmail. com, Blantyre.

Martinez wayamba game ya Chelsea atangolengezedwa lero lomwelino kt ndi osewela wa Chelsea nthawi you mweyo wapezeka mu ...
30/08/2026

Martinez wayamba game ya Chelsea atangolengezedwa lero lomwelino kt ndi osewela wa Chelsea nthawi you mweyo wapezeka mu first 11 ya Chelsea kuluza ndekuti chikhala chitoso kuwina ndekuti akhala akutamidwa

Cameroon inakanika kuzigulila mmalo kuchokera mu group stage yomwe munali ma team 12 kuphatikiza Malawi chifukwa choti C...
13/08/2026

Cameroon inakanika kuzigulila mmalo kuchokera mu group stage yomwe munali ma team 12 kuphatikiza Malawi chifukwa choti CAF imafuna kukhale ma team 16 anasankha ma team atatu chifukwa cha FIFA ranking omwe ndi Ivory coast, Egypt and Cameroon yomwe yafika finals

pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa

11/08/2026

mavuto a scorchers

1.kuchinyisa koyambilira tikukanika kupanga control pressure first 10 minutes
2.ma Arial balls (wa mmwamba) ma defender ukumawavuta kudula Game ya Egypt anachinya cha Head ya Ghana cha offside chija chinalinso chosumbilamo
3.kugwilisa ntchito ma Set peaces like ma Kona kick kukutivutabe Kusogolo kuja kuli madolo oti kumawapasa mipila yabwino azingosumbilamo
4.pena ngakhale ndi vuto losaonekela kwambiri tikumazasiilana kumaka kujejemesana tokhatokha
5. Goalkeepers trainer Ali ndi ntchito ngakhale last game zinali bwino koma sizoti tikukhulupililapo bwinobwino pa Golopo koma pot ndi mpira tiwalimbikise zabwino nde ndi zambili kuposa mavuto ochepa tatchulawa
pangan follow page ino kt zisamakuphonyen@

Mulungu anatibisila mmawa osamatha mawupangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
10/08/2026

Mulungu anatibisila mmawa osamatha mawu

pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa

10/08/2026

Fazili sakumaima pa touch line chifukwa alibe license osati ndi kunyada tikunvana kumeneko
pangan follow page ino

Mulungu anatibisila mmawa muli naye mangawanso ngt ? follow this page
10/08/2026

Mulungu anatibisila mmawa muli naye mangawanso ngt ?

follow this page

09/08/2026

Game yatha koma ngt tisagone eti?😂😂

chipogwetu akuti yachitipayo ndi Honda freed
09/08/2026

chipogwetu akuti yachitipayo ndi Honda freed

silver yasegula gap ya 2 points pamwamba pa wanderers yomwe yaphovomoka pa top atakhalapo kwa masabata awiripangan follo...
08/08/2026

silver yasegula gap ya 2 points pamwamba pa wanderers yomwe yaphovomoka pa top atakhalapo kwa masabata awiri

pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa

08/08/2026

wanderers yataya 3 points yokomola kale mmalo mophelatu moyale inasisimuka mpaka kubweza chigoli cha kumapetopeto kt ithele 1-1

Address

Mondiwadalitso@gmail. Com
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Za masewelo Mchichewa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category