Francis Arex Kambadya

Francis Arex Kambadya Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Francis Arex Kambadya, Sports, Zomba city, Blantyre.

15/10/2024

🤣🤣🤣🤣

02/06/2024
10/06/2023

Match Day!

🏆TNM Super League
⚽️Extreme FC vs Mighty Mukuru Wanderers FC
🗓Saturday 10 June 2023
🏟Bingu National Stadium
🕝2:30pm

09/06/2023

Panopa ndasiya kudya mbatata ndzingodya yootcha basi😂😂😂

02/06/2023

Good morning 🌄 guys

11/05/2023

MASEWERO A SILVER STRIKERS NDI MIGHTY TIGERS AWALEPHERETSA

Bungwe loyendetsa ligi yaikulu m'dziko muno la Super League of Malawi (Sulom) lalepheretsa masewero omwe amayenera kukhalapo loweruka lino pakati pa Silver Strikers ndi Mighty Tigers mu mpikisano wa TNM super league.

Malingana ndi bungweli, bwalo la Bingu lomwe limayenera kuchititsa masewerowa likhala lotsekedwe kuti lidzagwiritsidwe pa zochitika zokumbukira mtsogoleri wakale wa dziko lino Dr Kamuzu Banda.

23/04/2023

Bullets team to face Mafco at Kamuzu Stadium.

XI|
Richard Chimbamba ©️, Blessings Mpokera, Kesten Simbi, Clyde Senaji, Alick Lungu, Frank Willard, Mike Mkwate, Ernest Petro, Patrick Mwaungulu, Lanjesi Nkhoma and Maxwell Phodo.

SUBS|
Rabson Chiyenda, Nickson Nyasulu, Collins Okumu, Precious Phiri, Henry Kabichi, Chawanangwa Gumbo, Righteous Banda, Anthony Billiat and Ephraim Kondowe.

22/04/2023

End of the Match
Eagles 0-1 Silver
🏆

Arex Sports Update

22/04/2023

Kaswili mbambande amene wakakha chikopa lero kuposa azake onse pa masewelo a Noma ndi asilikali akuzomba

Christopher Kumwembe for Noma

Address

Zomba City
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Francis Arex Kambadya posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category