05/05/2026
🚨Ochemelera timu ya Real Madrid opotsa 1 million asaina dandaulo lofuna kuti Kylian Mbappe achoke ku timu ya Real Madrid.
Ma lipoti akuti Mbappe mkhalidwe ndi lomwe lavuta pomwe akuti ananamizila kuti ndi wovulala chonsecho anapita ku zinjoyi ndi chibwenzi chake.
Kuwonjezera apo, ochemelerawa akuti, maseweredwe a Mbappe ndi zomwe ankayembekezera mwa iye sizikugwilizana.
Kylian Mbappe wachinya zigoli 85 pa masewero 100 omwe wasewera ku timu ya Real Madrid.(Innoma journalist)