Nyóboy mw

Nyóboy mw Rodriguez nyondo nr 😎😎

🤔currently based on karonga

23/01/2023

In this world we come and Go osamaiwala

16/01/2023

Kudzuka ndi moyo ndichinthu cha mtengo wapatali ngati tadzuka ndi moyo tiyeni timuyamike mulungu
🙏🙏🙏

31/12/2022

Happy new year yearrrrrrrr😚😚😚🔥🔥🔥

11/12/2022

ODARA NDIYE OYENDA NDI YESU CHRIST
👏👏👏

03/12/2022

KUTEMBENUKA MTIMA UKADALI NDI MOYO NDICHINTHU CHOFUNIKA KWAMBIRI ZEDI PA MOYO WA MUNTHU.😄🤩😍👏👁️

27/11/2022

Zikomo ndaonanso kuwala kwa dzuwa tsku lalero mutamandke mukwezeke💜💚💙👏

26/11/2022

Osatekeseka anthu akamakamba zaiwe. mkango suchewuka phokoso la agalu. Mulungu ndi wamphavu kuposa satana
🙏🙏

23/11/2022

It's very important to know yourself because knowing yourself will help you find purpose and meaning for living in this world 💜 say no to su***de find yourself and know yourself 💜

Good 9t😍 God be with you

20/11/2022

Ndakusowani anthu a MULUNGU HAVE BLESSED NIGHT🤡

17/11/2022

Inuyoo mene mwangodzuka ndi moyo chonchomo ndi umboniisoo wawukuluso kwambiri umene
wakuonetserani

Address

Balaka

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nyóboy mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Nyóboy mw:

Share