Malawi Daily

Malawi Daily To be proud of learning is the greatest ignorance🤐
(1)

27/07/2026

Mupwetekanatu 🤣🤣🤣

27/07/2026

Kucheza kwa bwanji uku 🤣🤣🤣

27/07/2026

Koma kwa Rick pac nako kuli mavuto😂😂😂
Ada awa amakhala srs kungoti Rick anangowadzolowera basi🙌

27/07/2026

Babe tanditumizireko 50 pin yaku saloon,Ok dikira kaye ndiwone.Kodi boys mumakhala mwasiya kuona???🤣🤣🤣

Zikatero mumakagulira nthawi yanji?
27/07/2026

Zikatero mumakagulira nthawi yanji?

Lero kuli ma Birthday Happy birthday Chippie Uwah🎊🎁
27/07/2026

Lero kuli ma Birthday
Happy birthday Chippie Uwah🎊🎁

  Apolisi ya Chilipa m'boma la Mangochi amanga bambo wazaka 29 yemwe dzina lake ndi Jafali M'bwana pomuganizira kuti wap...
27/07/2026


Apolisi ya Chilipa m'boma la Mangochi amanga bambo wazaka 29 yemwe dzina lake ndi Jafali M'bwana pomuganizira kuti wapha bambo wina yemwe amapanga chibwezi ndi mkazi wake.

Mneneri wa polisi m'boma la Mangochi Amina Daudi wati apolisi apeza kuti malemuwa, Sumaila Aubrey anali pa ubwezi wamseli ndi mkaziyu.

"Ndipo patsikuli malemuwa anapita kunyumba kwa mkaziyu popeza mamuna wa mkaziyu anali ali Ku Lilongwe ndipo amayesa ngati sabwera. Koma mamunayu anatulukira mwadzidzi usiku ndipo anathyola chitseko ndikulowa mnyumbamo atawona kuti sakumutsekulira," anatero Daudi.

Daudi wati mamunayu anapeza mkazi wake akugonana ndi malemuwa ndipo iye anatenga mpeni ndikubaya pamtima pa malemwa omwe anakafela panjira atakwanitsa kuthawa mnyumbamo.

Bola Chikondi basi🔥🔥🔥🙌
27/07/2026

Bola Chikondi basi🔥🔥🔥🙌

Ma Driver mulikuti tidziwane apa kodi Neutral ali pati apa?🙄
27/07/2026

Ma Driver mulikuti tidziwane apa kodi Neutral ali pati apa?🙄

Happe birthday Andrea🔥🔥🔥
27/07/2026

Happe birthday Andrea🔥🔥🔥

Address

Blantyre

Telephone

+265996020480

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Daily:

Shortcuts

Share