24/05/2026
Maule anzanga,, ndi angati mwa inu amene mukufuna kuti katswiri Mike Digital Mkwate waluso ngati Chiomba Nkhanga awonjezere contract yake ndi FCB Nyasa Big Bullets? Ngati mulipo takwezani dzanja tikuoneni.
Mind you kuti ubale wa Mike Digital Mkwate ndi FCB Nyasa Big Bullets wafika kumapeto kwenikweni tsopano koma ma report akuonetsa kuti akukambirana zowonjezera mgwirizano wina watsopano ndi akulu akulu athu.
Osaiwala kupanga follow π Bullets Forever page kuti zabwinozi zisakuphonyeni Maule anzanga π₯π₯π₯π₯π₯
β€οΈπ€β‘π₯