29/11/2023
Ma********on (kubunyula kuzigona wekha)
Ma********on ndi mchitidwe oipa kwambiri umene achinyamata akumanga masiku ano pongofuna kuzisangalatsa mwa iwo okha koma ziwani kuti mchitidwe umeneu ndi ochokela kwa satana pongofuna kumutalikisani ndi mulungu komaso kukugwilitsa ntchito pa zofuna zake
Kodi ndizoipa bwanj?
Kubunyula ndi chimo komaso kumaononga umoyo wa munthu chifukwa munthu amene wazolowela kubunyula amazazidwa ndi ziwanda zimene zimamulamulira kotelo samakhumba zogona ndi mkazi/ mamuna coz ziwanda zimenez zimakhala za nsanje . Kotelo kupeza mkazi/mamuna wachibwez/banja silimachedw kutha.
Komaso ukazolowela mchitidwe umeneu kugona ndi mkazi sumava kathu chifukwa pathawi yomwe ukubunyula manja amakhala ulimba kotelo misepha ya chida chanu imakhala ikupelepeseka!
Ziwanda zimenez zimakhala zikuyamwa ma s***m pa thawi imeneyi kumapitisa kumidima kumakapangila zofuna zawo.
Zikatelo umakhala munthu osowa mtendele mmoyo wako komaso zimalanda mwayi wako kukusiya uli mmavuto azaoneni