Mighty Angerezi Media

Mighty Angerezi Media ⚽Official fan page ya Mighty Wanderers FC | πŸ”₯ Latest football updates & vibes | πŸ’™ One team, one family
(4)

04/09/2026
Simba Sporting Club yanyamuka ku Tanzania kudzera pa bwalo la ndege la Julius Nyerere International kubwera kuno ku  Mal...
04/09/2026

Simba Sporting Club yanyamuka ku Tanzania kudzera pa bwalo la ndege la Julius Nyerere International kubwera kuno ku Malawi.

Simba ikuyembekedzereka kusewera ndi Mighty Wanderers lamulungu likudzali pa masewero oyamba a mpikitsano wa CAF Champions league pabwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe.

Timuyi ifika m'dziko muno nthawi ya 9:00 mamawa uno pa bwalo la ndege la Kamuzu International.

Source:(Timveni sports desk)

 Potengera ndi ma lipoti omwe ndapeza ine, team yathu ya Mighty Wanderers FC ikulingalila zosiyana ndi Katswiri wakusogo...
04/09/2026


Potengera ndi ma lipoti omwe ndapeza ine, team yathu ya Mighty Wanderers FC ikulingalila zosiyana ndi Katswiri wakusogolo Christopher Jaccama Kumwembe kamba kosiyana zochitika ndi team yi.

Kumwembe amayembekezera kuyamba zokonzekera ndi team yi chichokereni Ku Green Buffalo ya dziko la Zambia komwe anali pa loan, koma katswiriyi chibwerereni Kuno Kumalawi sanapezekepo Ku zokonzekera za team yi ndipo kafukufuku wathu waonesa kuti katswiriyi akufuna ndalama zochuluka Kuti akhalebe Ku team yi.πŸ₯±πŸ§“

Pali Mwayi ochuluka oti Katswiriyi sakhala Ku team yi ndipo malipoti ena akusonyeza kuti katswiriyi wasaina Pre-contract ndi team ya Bullets πŸ˜….

⚽Mighty Angerezi Media-keeping the Nomads Spirit Alive !βœŠπŸ’™πŸ€πŸ’™

04/09/2026

πŸ₯΄

03/09/2026

Sama Tanjong ndi player wachabeπŸ‘ πŸ‘€ ambiri inu mumamuona mutalawa Mowa wamasese ndikuona mumamudaπŸ₯±πŸ§“πŸ₯΄πŸ˜πŸ™ˆ

Nginde ataikunga chotere we can confirm kuti Simba SC tingamuzepule mwakhaza πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ€£ 16. DALITSO KHUGWA  12. STANLEY SANUD...
03/09/2026

Nginde ataikunga chotere we can confirm kuti Simba SC tingamuzepule mwakhaza πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ˜€πŸ€£


16. DALITSO KHUGWA


12. STANLEY SANUDI
15. ALEX YONGO KAMBILINYA
13. TIMOTHY SILWIMBA


6. DANIEL KODONTO JNR
8. BLESSINGS SINGINI
17. ISAAC CHAIR KALIAT
10. GADDIE CHIRWA
19. WALLACE ADAM


7. SAMA TANJONG
30. CLEMENT NYONDO


24. CHANCY MTETE
22. EMMANUEL NYIRENDA
14. PETER THUSO NG'AMBI
2. MASIYA MANDA
11. MPHATSO KAMANGA
33. DALITSO NICO NAHIPA
35. RAJAB NYIRENDA
25.FELIX ZULU
9. PROMISE KAMWENDO
21. LAMECK MITHI
29. MUHAMMAD SULUMBA

πŸ₯±Simba SC ingausake ndi ma tochi πŸ§“πŸ₯΄πŸ˜πŸ˜

Kuionera Patali utha kumaona ngati ndi team yeniyeni koma ai ndithu Matapwisi enieni zikhatambwilo za team kapena kuti m...
03/09/2026

Kuionera Patali utha kumaona ngati ndi team yeniyeni koma ai ndithu Matapwisi enieni zikhatambwilo za team kapena kuti ma Agent a Airtel MoneyπŸ₯±πŸ§“πŸ˜πŸ‘

Uyuyu Sunday lino tizamuphetemuka chakwawo leka Watipeza nthawi yolakwika πŸ˜†πŸ˜πŸ˜†

πŸ˜‚Koma INU uyuπŸ€£πŸ‘
03/09/2026

πŸ˜‚Koma INU uyuπŸ€£πŸ‘

⚽ THROWBACK THURSDAYTHE MIGHTY WANDERERS OF OLD! πŸ”΅βšͺπŸ‘ŽThere was a time when watching Mighty Wanderers was more than just f...
03/09/2026

⚽ THROWBACK THURSDAY
THE MIGHTY WANDERERS OF OLD! πŸ”΅βšͺπŸ‘Ž

There was a time when watching Mighty Wanderers was more than just football it was an experience! πŸ”₯

Legends, packed stadiums, passionate supporters and unforgettable battles made Malawi football special. πŸ‡²πŸ‡Όβ€οΈ

Question for the OGs: πŸ‘€
πŸ‘‰πŸΎ Which Mighty Wanderers player from the old days was your favourite?

πŸ‘‰πŸΎ And what year do you miss the mostπŸ‘€? πŸ§“πŸ₯΄βš½

⚽Mighty Angerezi Media-keeping the Nomads Spirit Alive!βœŠπŸ€πŸ’™πŸ€

03/09/2026

πŸŽ₯πŸ”΅βšͺ LET’S GO, ANGEREZI! πŸ’™πŸ€

This Sunday, let’s come together as one family and give our players all the support they need as Mighty Wanderers FC take on Simba SC in the CAF Champions League. πŸ†πŸŒβš½

This is not just an ordinary game β€” it’s an opportunity for us to show the true strength of The Nomads Family! πŸ”₯πŸ’ͺ

πŸ“£ If you are a true Mighty Wanderers FC supporter, you should be there! Let’s get behind our boys from the first whistle until the final whistle. πŸ’™πŸ€

EVERYONE TO THE STADIUM! 🏟️πŸ”₯
MIGHTY WANDERERS FC β€” WE ARE ONE! πŸ’™βšͺ

πŸ˜ŠπŸ™Come on, Nomads!

⚽Mighty Angerezi Media-keeping the Nomads Spirit Alive! βœŠπŸ’™πŸ€πŸ’™
πŸ‘Š

Address

Machinga
Ntaja

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mighty Angerezi Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share