15/09/2026
Koma mwakonzekaaaaaa!!!!
Konse komwe muliko, dziwani kuti lero pa 15 September 2026, nditsiku lofunika kwambiri kuno kwathu kumadzulo kwa Dedza ija timati Dedza dzalanyama constituency.
Izi ndi kaamba ka zitukuko ziwiri zomwe zikudzakhazikitsidwa ndi mp wanu uja okondedwa, Hon Morris Chikafa, mtumiki wanu wanyengo zonse yemwe tsopano ndi wa Malawi congress party.
Zitukukozi ndi za nsewu wathu wa Livinza- mtambalika-Njonja- Chibwezo- Mikondo via Ndevu ku Chimoto ward komaso Mofati via Majamanda ku kafere ward.
Nayoso bursary ya 150 000 000 .00 tikumaliza lero kulandila ma fomu kwa ana a sukulu za secondary za Umbwi, Mayani, Blantyre sec school, Robert brake, Mzuzu government sec school, Chimphalika CDSS komaso Chawa CDSS.
Kwa okhawo amwe adasankhidwa panopa ngakhale amene akayamba folomu 2, ali folomu 3 komaso ali folomu 4 mwai uja ndi umenewu, musatsalire kumbuyo, anzanu apereka kale ma fomu awo.
Chikafa uja, atitumikira ndithu tien, tithandizepo pakusintha dera lino!!!