Bwalo La Mapale - Maule Fans

Bwalo La Mapale - Maule Fans 𝐅𝐂𝐁 ππ˜π€π’π€ ππˆπ† 𝐁𝐔𝐋𝐋𝐄𝐓𝐒 𝐅𝐀𝐍𝐒 𝐋𝐄𝐓'𝐒 𝐆𝐀𝐓𝐇𝐄𝐑 𝐇𝐄𝐑𝐄 οΏ½οΏ½ ❀️♨️πŸ”₯β™¨οΈβ€οΈβ™¨οΈπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌπŸ‡²πŸ‡ΌοΏ½οΏ½

30/08/2026

Cow πŸ„ Boys 2-1 CAF

🀣

πŸ“… Tikubwerera ku Mpira Stadium. Patangopita sabata imodzi kuchokera pamene timakumana mu Airtel Top 8, Tikhale tikubwere...
14/07/2026

πŸ“… Tikubwerera ku Mpira Stadium.

Patangopita sabata imodzi kuchokera pamene timakumana mu Airtel Top 8, Tikhale tikubwerera ku Mpira Stadium kukakumana ndi Ekhaya FC mu FDH Bank Premiership.

πŸ“– Werengani zambiri:https://nyasabigbullets.com/fixtures/ekhaya-next-as-bullets-turn-focus-to-league-response.

Bullets switch focus back to the FDH Bank Premiership with an away trip to Ekhaya as The People's Team look to extend the unbeaten league run

πŸ”΄ Tsiku la Masewera.Mphindi zina 90. Malo amodzi mu semifinals.
11/07/2026

πŸ”΄ Tsiku la Masewera.

Mphindi zina 90. Malo amodzi mu semifinals.

LERO NDI TSIKU LIMENE KASWIRI WATHU GEORGE CHAOMBA ANABADWA LET'S WISH HIM A HAPPY BIRTHDAY πŸŽ‚
09/07/2026

LERO NDI TSIKU LIMENE KASWIRI WATHU GEORGE CHAOMBA ANABADWA LET'S WISH HIM A HAPPY BIRTHDAY πŸŽ‚

πŸ“Œ NEXT MATCH πŸ†š EKHAYA FC🏟️ MPIRA STADIUM KICK-OFF TIME 14:30 PM CONE ON MAULE
09/07/2026

πŸ“Œ NEXT MATCH πŸ†š

EKHAYA FC

🏟️ MPIRA STADIUM

KICK-OFF TIME 14:30 PM

CONE ON MAULE

Ndichimenecho maule πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯ Lero chatinyamula ichiiiii Ephraim Kondowe 2 goals kukhalatso man of the match      ...
04/07/2026

Ndichimenecho maule πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Lero chatinyamula ichiiiii Ephraim Kondowe

2 goals kukhalatso man of the match

KHAAAAAAAAA KHOOOOOOOO Waishosha FDH Bank PremierShip Back To Back Wins
04/07/2026

KHAAAAAAAAA KHOOOOOOOO

Waishosha FDH Bank PremierShip

Back To Back Wins

FCB Nyasa Big Bullets Fc Training Update ahead of FDH Bank Premiership Match against Creck Sporting tomorrow at Mpira St...
03/07/2026

FCB Nyasa Big Bullets Fc Training Update ahead of FDH Bank Premiership Match against Creck Sporting tomorrow at Mpira Stadium
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή

GOALKEEPERS
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
McLean Mwale
Pilirani Mapira
Julius Banda
Innocent Nyasulu

DEFENDERS
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
Ahmad Kung'unde
Khumbo Banda
Yamikani Mologeni
Aaron Chilipa
Blessings Mpokera (C)
Henry Chiwaya
Edward Thengo
Emanuel Kaunga
Andrew Jovinala

MIDFIELDERS
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
Yankho Singo
Frank Willard
Chawanangwa Gumbo
Madalitso Safuli
Prince Chiumia
Wongani Lungu

ATTACKERS
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
Peter Banda
Mike Mkwate
Clever Kalambo
Misheck Billiat
Sean McBrams

STRIKERS
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
Gasten Phodo
Ephraim Kondowe
Dastan Banda
Hassan Kajoke
George Chaomba

βœ… Injuries
πŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡ΉπŸ‡¦πŸ‡Ή
Paul Master

🎯 Tineneso pano kuti osewera kumbuyo kwatimuyi Ahmad Kung'unde amene anali ovulala tsopano wachira bwino bwino ndipo wayamba training yamphamvu ndi azinzake. Titsimikizeso pano kuti osewera pakati mutimuyi Madalitso Safuli amene sanasewere nawo sabata yathayi tsopano alibwino ndipo atumikira nawo sabata ino ngati atapatsidwa mpata.

🎯 Mphunzitsi wamkulu kutimuyi Wedson Wadawada Nyirenda wati akukhulupilira zoti zigoli ziyamba kupezeka zambiri posachedwapa potengera ndimmene osewera akumapangira mipata yomwetsera zigoli. Nyirenda wayankhula izi pamsonkhano wa atolankhani ndipo anapitiliza kunena kuti osewera omwe alipo ndi akungofunika kuwaphunzitsa kudekha akafika malo oti achinye. Wadawada Nyirenda wati pakali pano alimbikitsa osewera omwe ali nawo kaye kuti mipata yogoletsa yambiri yomwe akumapeza aziyigwiritsa ntchito bwino bwino.

βœ… Tineneso pano kuti mphunzitsiyu yemwe akufunafuna mphangala yoti izimalizitsa ntchito yomwetsa zigoli,wadandaula ndikulephera kusaina Babatunde Adepoju chifukwa amamufuna kwambiri. Nyirenda wati mphunzitsi aliyese amakhala okhumudwa ngati osewera amene amamufuna wapita kutimu kwina komabe ndimmene zimakhalira chifukwa pamapeto pazonse osewera ndamene amasankha komwe akufuna ndipo anapitiliza kunena kuti zateremu ndekuti aponya maso kwa osewera ena amdziko muno komaso kunja kwadziko lino.

😍 Wadawada Nyirenda wapereka ulemu kwa masapota a Bullets amene wati amuonetsera chikondi lolemba lapitali pa Mpira Stadium pomwe anamuyitana kuti akamupatse moni. Nyirenda wati zimenezi ndizofunikira kwambiri chifukwa zamulimbikitsa kwambiri ndipo anati sapota amafuna kupambana nthawi zonse kotero kuti alimbikitsa osewera ake kuti ayikilepo mtima chifukwa masapota amalipira ndalama pageti kuti awone timu yawo ikupambana...

πŸ–οΈ Masana abwino Mapale kulikonse komwe muli ndimakunyadirani kwambiri. Ine ndiyemwe uja die hard wamkulu.

πŸ–οΈ
Maule4Life ❀️ ⚽ βœ…
🎯🎯🎯🎯🎯🎯🎯🎯

Wada Wada πŸ’ͺ🏻πŸ’ͺ🏻Mau amodzi maule
30/06/2026

Wada Wada πŸ’ͺ🏻πŸ’ͺ🏻

Mau amodzi maule

Frank Willard is back, ichichi kungoti ma injury amangochivuta koma ndi akatundu.Malo aja chatenga ndipo dzulo chagaza m...
30/06/2026

Frank Willard is back, ichichi kungoti ma injury amangochivuta koma ndi akatundu.
Malo aja chatenga ndipo dzulo chagaza mpira osat masewera.

Address

Mzuzu
ZIP

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bwalo La Mapale - Maule Fans posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category