03/04/2026
mpungwe pungwe ku mzuzu city hammers... pamene prayer otchedwa Yasin Rashid, amene amamenya pakati. akufunidwa kuma team osiyana siyana kuphatikizapo Kamuzu bracks KB, Dedza Goshen ndi chitipa united... Koma mzuzu city hammers yakanitsitsa kuti prayer yu singamupititse ku team iliyonse chifukwa alinaye contract yayikulu. Koma izi zabweletsa mpungwepugwe pamene Yasin Rashid wayankhula kuti "mzuzu city hammers yamumenyetsa zaka zambiri osamulipira ndeno Ali ndiufulu opita ku team iliyonse olo apoayi kusiya kusewela mpira mpaka contract yake izathe...π