Mudzi Wakungi

Mudzi Wakungi Sharing news abut football is our aim ⚽ ⚽ ⚽ ⚽ ⚽

Christiano RONALDO wanena kuti 2026 World cup ikhala yomaliza kumenya mu mpikisano umenewu wa World cup chifukwa alibe z...
11/11/2025

Christiano RONALDO wanena kuti 2026 World cup ikhala yomaliza kumenya mu mpikisano umenewu wa World cup chifukwa alibe zaka Zambiri akusewerabe mpira.

Arsenal next 3 fixtures koma akungi anthuwa apwetekana awa.
11/11/2025

Arsenal next 3 fixtures koma akungi anthuwa apwetekana awa.


No player has made more interceptions than Moisés Caicedo (26) in the Premier League this season.Akungi mukuona bwa? Ich...
11/11/2025

No player has made more interceptions than Moisés Caicedo (26) in the Premier League this season.
Akungi mukuona bwa? Ichi tidya nacho bwinotu


Since the start of this season BRENTFORD ndiyo yagoletsa zigoli za mbiri(9) from throw-in. Koma awa apweteka ma team.
11/11/2025

Since the start of this season BRENTFORD ndiyo yagoletsa zigoli za mbiri(9) from throw-in.

Koma awa apweteka ma team.


LIVERPOOL manager ARNE SLOT Wang'ambitsa kale ma TICKET akungi kuposa ndi mene anang'ambitsira season yonse yathayi.Akun...
11/11/2025

LIVERPOOL manager ARNE SLOT Wang'ambitsa kale ma TICKET akungi kuposa ndi mene anang'ambitsira season yonse yathayi.
Akungi Koma ziyendapo apa?


Ichichi chafika ndi Ma Set avutawa.Akungi Nyimbo ikhale Ma Set
11/11/2025

Ichichi chafika ndi Ma Set avutawa.
Akungi Nyimbo ikhale Ma Set

Zoti Akusewera mpira zosawakhuza ayi ndithu Kudya Apple FODEN and HALAAND.Real meaning of Phweteko
10/11/2025

Zoti Akusewera mpira zosawakhuza ayi ndithu Kudya Apple FODEN and HALAAND.

Real meaning of Phweteko


Akungi akuti sakuchotsa tsitsi mpaka FLORIAN WIRTZ atagoletsa Premier league goal komatu akungi.
10/11/2025

Akungi akuti sakuchotsa tsitsi mpaka FLORIAN WIRTZ atagoletsa Premier league goal komatu akungi.


Kwacha bwanj akungi tiyeni tiyeseso.Koma ichichi anthu akuchitama kuti chadyetsa bwino anthu.
10/11/2025

Kwacha bwanj akungi tiyeni tiyeseso.
Koma ichichi anthu akuchitama kuti chadyetsa bwino anthu.


FT: MANCHESTER CITY 3-0 LIVERPOOL After week 11 in EPL yanu ili pat?
09/11/2025

FT: MANCHESTER CITY 3-0 LIVERPOOL

After week 11 in EPL yanu ili pat?


09/11/2025

63' Khooooo!!!!!! DOKU!!! MAN CITY 3-0 LIVERPOOL

09/11/2025

HT: MANCHESTER CITY 2-0 LIVERPOOL

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mudzi Wakungi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category