Malawi sports LIVE

Malawi sports LIVE ๐„๐ฑ๐ฉ๐ž๐ซ๐ข๐ž๐ง๐œ๐ž ๐ญ๐ก๐ž ๐ญ๐ก๐ซ๐ข๐ฅ๐ฅ ๐จ๐Ÿ ๐ฅ๐ข๐ฏ๐ž ๐Ÿ๐จ๐จ๐ญ๐›๐š๐ฅ๐ฅ ๐ฐ๐ข๐ญ๐ก ๐Œ๐š๐ฅ๐š๐ฐ๐ข ๐’๐ฉ๐จ๐ซ๐ญ๐ฌ ๐‹๐ˆ๐•๐„! ๐‰๐จ๐ข๐ง ๐จ๐ฎ๐ซ ๐œ๐จ๐ฆ๐ฆ๐ฎ๐ง๐ข๐ญ๐ฒ ๐Ÿ๐จ๐ซ ๐ฆ๐š๐ญ๐œ๐ก ๐ฎ๐ฉ๐๐š๐ญ๐ž๐ฌ, ๐ฌ๐œ๐จ๐ซ๐ž๐ฌ, ๐š๐ง๐ ๐ฌ๐ฉ๐จ๐ซ๐ญ๐ฌ ๐๐ข๐ฌ๐œ๐ฎ๐ฌ๐ฌ๐ข๐จ๐ง.

Caf Women's Champions League Semifinal Zesco Ndola girls imawona ngati sikucha iphodedwa leroSilver Strikers ladies ๐Ÿ†š Ze...
27/08/2026

Caf Women's Champions League Semifinal
Zesco Ndola girls imawona ngati sikucha iphodedwa lero

Silver Strikers ladies ๐Ÿ†š Zesco Ndola girls

Kwangotsala masiku atatu Kodi inu mwagula kale
26/08/2026

Kwangotsala masiku atatu Kodi inu mwagula kale

Silver Strikers ladies ili ndime ya Semifinal ku mpikisano wa Cosafa Women's Championship pomwe mawa osewera ndi Zesco N...
26/08/2026

Silver Strikers ladies ili ndime ya Semifinal ku mpikisano wa Cosafa Women's Championship pomwe mawa osewera ndi Zesco Ndola girls pofuna kudzigulura malo mu ndime yotsiliza

Nsingizini HotSpurs yaphodedwa komaso ayisandutsa bankerSilver Strikers ladies 5-1 Nsingizini HotSpurs
25/08/2026

Nsingizini HotSpurs yaphodedwa komaso ayisandutsa banker

Silver Strikers ladies 5-1 Nsingizini HotSpurs

According to Twaha Chimuka striker John mchema has terminated his employment contract with Kamuzu Barracks FC to join Ek...
25/08/2026

According to Twaha Chimuka striker John mchema has terminated his employment contract with Kamuzu Barracks FC to join Ekhaya FC and is expected to get a sum of 10 million Kwacha as signing on fee

Bungwe la Super League of Malawi (SULOM) lati lamaliza kulandira ma umboni pazazomwe zidachitika pamasewero a Creck Spor...
25/08/2026

Bungwe la Super League of Malawi (SULOM) lati lamaliza kulandira ma umboni pazazomwe zidachitika pamasewero a Creck Sporting Club ndi Ekhaya FC ndipo lati lipereka chigamulo posachedwapa.

Masewero atatha kudali kusinthana zibakera pakati pa akulu akulu a timu ya Ekhaya komaso Creck Sporting Club

Nduna ya zamasewero mdziko la South Africa Gayton McKenzie yalembera kalata bungwe loyendetsa mpira dzikolo la South Afr...
25/08/2026

Nduna ya zamasewero mdziko la South Africa Gayton McKenzie yalembera kalata bungwe loyendetsa mpira dzikolo la South African Football Association (SAFA) kuti libweze ndalama zokwana 13 million rand zomwe lidalandira Kuti libweretse makina aja a video assistant referee (VAR).

McKenzie wati ndi okhumudwa ndi SAFA kuti sidakwanilitse kubweletsa VAR mu ligi ya mdziko la South Africa ndipo wapeleka masiku 21 kuti SAFA ibweze ndalamazi.

Ndipo McKenzie ati adalembera kale kalata bungwe la FIFA kuti liwathandize kubweletsa VAR mu mdziko la South Africa

Timu ya Silver Strikers ladies dzulo yagonja ndi zigoli zitatu kwa duu ndi timu ya Mamelodi Sundowns.Koma the central ba...
24/08/2026

Timu ya Silver Strikers ladies dzulo yagonja ndi zigoli zitatu kwa duu ndi timu ya Mamelodi Sundowns.

Koma the central bankers ili ndi umwayi ofika Semifinal ngati izagonjetse Nsingizini HotSpurs lachiwiri lino

Yanuyo yokondwedwayo ili pati
23/08/2026

Yanuyo yokondwedwayo ili pati

FDH Bank Premiership results today
23/08/2026

FDH Bank Premiership results today

Address

Lilongwe

Telephone

+265888964698

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi sports LIVE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi sports LIVE:

Shortcuts

Share