21/01/2017
Kusatira kudwala kwa wosewera wakale wa team ya Big bullets and Dwangwa united Lunda, page ndi group lathu latengapo mbali k*tolera limodzi limodzi k*t tikam***andize pomwe pakali pano wagonekedwa pa chipatala cha kamuzu central.
Kwa omwe angafune k*thandizapo atha k*tifikira kuzera pa airtel money 0995168469, mpamba 0884443730 or National Bank acc number 3710025, kwa omwe ali kunja kwa dziko lino m***a k*tifikira pa mukuru or money gram.
Anthu okwana 27 omwe ali pama group a whatsapp apereka k54200 kufikira lero pa 21/01, tikhalebe tik*tolera mpaka sabata la mawa pa 25 January pomwe tizasakhe anthu okamuona. Ak*torera ndalama ndi Kasanga Ronard Thews.
For any queries use numbers above to call or whatsapp. Xanks in advance.