Mavyete Pa Stand

Mavyete Pa Stand This is a sports interaction fan page

First round complete📊Songwe Border United and Extreme FC lead the way with 25 points each, while Changalume Barracks rem...
23/08/2026

First round complete📊

Songwe Border United and Extreme FC lead the way with 25 points each, while Changalume Barracks remain the only team yet to register a win.

Current standing in the FDH Bank Premiership
23/08/2026

Current standing in the FDH Bank Premiership

08/04/2026

The road to defending the crown begins on 25 April⚽️🏆🔥
Will Mighty Wanderers FC make an early statement?

Mpira wapakati pa ma timu a Mighty Wanderers ndi Kamuzu Barracks ukaseweledwa pa Bingu National Stadium.Malingana ndi bu...
22/12/2025

Mpira wapakati pa ma timu a Mighty Wanderers ndi Kamuzu Barracks ukaseweledwa pa Bingu National Stadium.

Malingana ndi bungwe la masewero a mpira la Super League of Malawi, mpirawu ukaseweledwa loweluka pa 27 December.

Pa tsikuli Mighty Wanderers ikapatsidwa nyota ngati akatswiri a TNM Super League.

Mavyete mwachilandila bwanji?

Nanga zoona ukatsiwiri wa TNM Super League kuwapatsila anzanu pa Balaka stadium? 🤣🤣🤣

Tiwalandile tiwalandile.Singing 🎤 Tiwalandile, alendo anthu abwela lero, tiwalandile.Awa ndi matimu amene akulowa mu TNM...
22/12/2025

Tiwalandile tiwalandile.

Singing 🎤

Tiwalandile, alendo anthu abwela lero, tiwalandile.

Awa ndi matimu amene akulowa mu TNM (Telekom Networks Malawi) Super League season ikubwelayi.

Tiwalandile.

Amuyedzeka? Mavyete zimayenera kutero kapena alakwitsa?
22/12/2025

Amuyedzeka?

Mavyete zimayenera kutero kapena alakwitsa?

Kuli chimwemwe chodzadza tsaya ku Manoma chifukwa timu ya an achisodzera ya Mighty Wanderers Youth itha kupezeka kuti ya...
22/12/2025

Kuli chimwemwe chodzadza tsaya ku Manoma chifukwa timu ya an achisodzera ya Mighty Wanderers Youth itha kupezeka kuti yatenga Blantyre District First Capital Bank U-19 League.

Izi zikudza kamba koti yapeza chipambano pamasewero omwe yagonjetsa timu ya Manchester Motor Spares 2-1.

Mmene zatelemu Mighty Wanderers Youth ikutsogola ndima pointi 54 mum'ndandanda wamatimu 16 kuchokera kumasewero 23 omwe yasewera.

Timu ya FCB Nyasa Big Bullets Youth ndiyomwe ili ya chiwiri ndi mapointi 46.

Pamene Ekhaya Youth ndiyachitatu pomwe yatolera mapointi 43 ndipo Manchester Motor Spares ili panambala ya chinayi ndi mapointi 40.

Mavyete pa stand mukumva bwanji mu mtimamo?

22/12/2025

League mwayiwona bwanji Mavyete?

Address

Victoria Avenue
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mavyete Pa Stand posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category