Business plug

Business plug Let's talk about football

Katswiri wa Chelsea walowela ku bayern Munich pa ngongole
02/09/2025

Katswiri wa Chelsea walowela ku bayern Munich pa ngongole

Katswiri wa mmbali wa man United walowela ku aston villa pa ngongole
02/09/2025

Katswiri wa mmbali wa man United walowela ku aston villa pa ngongole

Kuchoka ku abwenzi pano ndi adani pa mpira anali banja limodz pano anatenga njira zosiyana Anyway congrats wissa ku team...
02/09/2025

Kuchoka ku abwenzi pano ndi adani pa mpira anali banja limodz pano anatenga njira zosiyana

Anyway congrats wissa ku team yako yatsopano Newcastle United

Team ya leeds yapambadza team ya Everton usiku wa dzulo Leeds 1-0Everton Mmenemu ndimene zayendela dzulo
19/08/2025

Team ya leeds yapambadza team ya Everton usiku wa dzulo

Leeds 1-0Everton

Mmenemu ndimene zayendela dzulo

Nkhani yomwe yachema ku EnglandYoane Wissa wapanga unfollow Brentford,ndipo wasintha profile picture  to black and wacho...
18/08/2025

Nkhani yomwe yachema ku England

Yoane Wissa wapanga unfollow Brentford,ndipo wasintha profile picture to black and wachotsa ma photos ake onse pa instagram account yake pamene akuoneka ngati akufuna kuchoka ku club imeneyi.

Zinali motele dzulo ku England ๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡Manchester United yagonja pakhomo ndi team ija ya arsenal United 0-1arsenal Team ya Che...
18/08/2025

Zinali motele dzulo ku England ๐Ÿ‘‡๐Ÿ‘‡

Manchester United yagonja pakhomo ndi team ija ya arsenal
United 0-1arsenal

Team ya Chelsea yafananitsa mphamvu ndi timu ya Crystal palace atalephelana kuchinyana
Chelsea 0-0crystal palace

Team ya Nottingham yagagada team ya Brentford

Nottingham 3-1Brentford

Menemu ndimene zayendela dzulo ku England

16/08/2025
  Lero pa 16 August  umu ndi mene zayendela ku mangalandeWolves yagonja pakhomo ndi time ya Manchester city ku zigoli 4 ...
16/08/2025



Lero pa 16 August umu ndi mene zayendela ku mangalande

Wolves yagonja pakhomo ndi time ya Manchester city ku zigoli 4 kwa 0

Thomas frank zake zayamba bwino ndithu pamene timu yake ya Tottenham yapeza chipambano pogonjetsa burnley ndi zigoli 3 kwa o

Anyamata a Newcastle zawo sizinawayendele pamene afananitsa mphamvu ndi timu ya aston villa ngakhale aston villa inali ndi red card palibe amene anawona pa golo pa mdzake pamene masewela atela 0 kwa 0


West ham United yagonja ndi timu ya Sunderland yomwe yalowa kuchoka ku championship ndi zigoli 3 kwa 0

Brighton yafananitsa mphamvu ndi timu ya Fulham ndi zigoli 1 kwa 1

Mmenemo ndimene zayendela ku England
Ndipo mkhondo ilipo lipo mawa pamene arsenal ikukumana ndi Manchester United

Gyokeres vs sesko

Bournemouth machine adha awawa amaika effort pangolin wawa ndiamene ali a top score padakali pano  ๐Ÿšจ Premier League Top ...
16/08/2025

Bournemouth machine adha awawa amaika effort pangolin wawa ndiamene ali a top score padakali pano

๐Ÿšจ Premier League Top scorers! ๐Ÿด๓ ง๓ ข๓ ฅ๓ ฎ๓ ง๓ ฟโœจ

1๏ธโƒฃ ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญ Antoine Semenyo โ€“ โšฝโšฝ (2 Goals)
2๏ธโƒฃ ๐Ÿ‡ซ๐Ÿ‡ท Hugo Ekitike โ€“ โšฝ (1 Goal)
3๏ธโƒฃ ๐Ÿ‡ณ๐Ÿ‡ฑ Cody Gakpo โ€“ โšฝ (1 Goal)
4๏ธโƒฃ ๐Ÿ‡ฎ๐Ÿ‡น Federico Chiesa โ€“ โšฝ (1 Goal)
5๏ธโƒฃ ๐Ÿ‡ช๐Ÿ‡ฌ Mohamed Salah โ€“ โšฝ (1 Goal)

โœ…โšฝ๏ธ chigoli chake choyamba mu Premier league.โœ…๐Ÿ…ฐ๏ธ Assist yake yoyamba muPremier League .โœ…๐Ÿ† Award yake yoyamba mu premier ...
16/08/2025

โœ…โšฝ๏ธ chigoli chake choyamba mu Premier league.
โœ…๐Ÿ…ฐ๏ธ Assist yake yoyamba muPremier League .
โœ…๐Ÿ† Award yake yoyamba mu premier league

Pangolin wa liverpool Hugo Ekitike. ๐Ÿ”ด

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Business plug posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share