Sports news update

Sports news update . Daily fixturesLive game updates and results about 60 leaguesTransfer newsPredict tips

breaking newsTeam ya mpira wa miyendo ya Manchester City ya Ku mangalande ayipeza ndi milandu 114 mwa 115 yokhudza kuphw...
26/09/2026

breaking news

Team ya mpira wa miyendo ya Manchester City ya Ku mangalande ayipeza ndi milandu 114 mwa 115 yokhudza kuphwanya malamulo azachuma a Premier League.

Chigamulochi chaperekedwa ndi komiti yoyima payokha pambuyo pa kumva mlandu omwe unayamba mu September Chaka cha 2024.

Milanduyi ndiyoyambira m'chaka cha 2009 mpaka 2018, yokhudza kupereka malipoti abodza okhudza ndalama, kusafotokoza mokwanira ndalama zomwe osewera ndi makochi amalandira, komanso, kuphwanya malamulo a UEFA Financial Fair Play ndi ina yambiri.

Malipoti akuti zilango zomwe angapatsidwe ndi kuchotseledwa mapointi, kulipitsidwa ndalama kapena zilango zina zokhudza mpikisano, koma palibe chilango chomwe chaperekedwa pakadali pano.



Source: Punch news paper, BBC ndi the score+1

25/09/2026

Mibawa TV why??????😭😭😭

HT
25/09/2026

HT

flames line up
25/09/2026

flames line up

full timeBotswana vs MalawiMisheck Billiat has been awarded Man of the matchBotswana 0-3Malawi
21/09/2026

full time

Botswana vs Malawi
Misheck Billiat has been awarded Man of the match

Botswana 0-3Malawi

TWG Patamveka mpheketsera kudzera kuma group komanso ma page osiyana siyana kuti Christopher Jacama Kumwembe akupita ku ...
21/09/2026

TWG



Patamveka mpheketsera kudzera kuma group komanso ma page osiyana siyana kuti Christopher Jacama Kumwembe akupita ku team ya FCB Nyasa Big Bullets tisimikize pano kuti Kumwembe sakupita kulikonse.

Izitu zilichomwechi kamba kakuti osewerayu ndi team yake ya Mighty Wanderes amvana zonse zoyenera kuti osewerayu second round atumikire Manoma

❌ Deal Off yopita ku FCB Nyasa Big Bullets βœ… Deal on yopita ku Manoma

Flames head coach Kalisto Pasuwa has named his provisional squad for the 2027 AFCON qualifiers.Sports news update
14/09/2026

Flames head coach Kalisto Pasuwa has named his provisional squad for the 2027 AFCON qualifiers.

Sports news update

‼️πŸ”₯ Gerlad Phiri Jr: CAF Imafuna Osewera Odziwa International Football Osewela wakale Wa Flames Gerald Phiri Jr akunena ...
13/09/2026

‼️πŸ”₯ Gerlad Phiri Jr: CAF Imafuna Osewera Odziwa International Football

Osewela wakale Wa Flames Gerald Phiri Jr akunena kuti mateam aku Malawi akufuna kuchita bwino mu CAF competitions, ayenera kuyika ndalama zambiri posaina osewera apamwamba komanso omwe ali ndi international experience. Iye akuti masewera a mu CAF ndi osiyana kwambiri ndi a m’dziko muno, choncho kupita ku mpikisano wa ku Africa popanda osewera odziwa bwino masewera apamwamba kumangowononga ndalama ndi zinthu za timu.

Phiri Jr wapereka chitsanzo cha Stanley Sanudi kuti ndi mmodzi mwa osewera omwe ali ndi international experience yokwanira, pomwe ena onse pa Osewela a Wenderers alibe experience yosewelela CAF.

Malinga ndi iye, kugonjetsedwa kwa 6–1 ndi Simba ndi chitsanzo chowonekera cha kusiyana kwa experience ndi quality yomwe ikufunika pa CAF. πŸ‡²πŸ‡Όβš½

Coach McDonald Mtetemera makes three changes to the starting eleven:πŸ”΅ Kudonto Jnr, Kamanga and Sulumba drop to the bench...
13/09/2026

Coach McDonald Mtetemera makes three changes to the starting eleven:
πŸ”΅ Kudonto Jnr, Kamanga and Sulumba drop to the bench for Zulu, Kamwendo and Mithi

Sports news update

π’πˆπ‹π•π„π‘ π’π“π‘πˆπŠπ„π‘π’ π€πππŽπˆππ“π’ 𝐀𝐍 πˆππ“π„π‘πˆπŒ π“π„π‚π‡ππˆπ‚π€π‹ 𝐏𝐀𝐍𝐄𝐋Silver Strikers Football Club wishes to inform its valued supporters,...
09/09/2026

π’πˆπ‹π•π„π‘ π’π“π‘πˆπŠπ„π‘π’ π€πππŽπˆππ“π’ 𝐀𝐍 πˆππ“π„π‘πˆπŒ π“π„π‚π‡ππˆπ‚π€π‹ 𝐏𝐀𝐍𝐄𝐋

Silver Strikers Football Club wishes to inform its valued supporters, partners, and the wider football fraternity that it has established an interim Technical Panel to oversee the Main Team’s affairs with immediate effect.

The interim Technical Panel is as follows:

Sports news update

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Sports news update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category