KUMA STAND

KUMA STAND Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from KUMA STAND, Sport & recreation, Chilomoni, Blantyre.

KUMA STAND is a proffessional Sports and recreation Page which covers all sports News and live Broadcast from several Major Stadiums across Malawi and The whole world, this includes...
Fixtures,live Results, KUMA STAND PODCAST, and Transfer Update

Yanuyo ili pati
22/07/2026

Yanuyo ili pati

22/04/2026

A Ref nthawi🤭

Week yoyambira   tikhala tili mabwalo amenewa kuchitira umboni mene masapota Atamwele wamkaka   onsiyanasiyana muno mmal...
22/04/2026

Week yoyambira tikhala tili mabwalo amenewa kuchitira umboni mene masapota Atamwele wamkaka onsiyanasiyana muno mmalawi ndikutitu inu mu FDH BANK premiership....

Ife chete   kudikila yowinayo timbwembwedzere tizipita Stand yomwe ikukomayo koma inu pa Stand pa
18/04/2026

Ife chete kudikila yowinayo timbwembwedzere tizipita Stand yomwe ikukomayo koma inu pa Stand pa

18/04/2026

Manoma nde akuti ailandira Bata muchaka cha 2026 akufuna amalizise pomwe aasiira hhhmmm

18/04/2026
18/04/2026

pa Stand lero pachema

16/04/2026

Tinapanga kaye zii pakatipa kuti tikoze pena ndi pena league isanayambe chifukwa chaka chino zilikotu

25/03/2026

Ndikuti Kwangosalatu Mwenzi umodzi okha Bwede chikadzat.....

Mndandanda wa Anyamata osewera mpira wa miyendo wa dziko lino okwana 25 Omwe akukatenga nawo gawo mumpikisano wa  4 NATI...
25/03/2026

Mndandanda wa Anyamata osewera mpira wa miyendo wa dziko lino okwana 25 Omwe akukatenga nawo gawo mumpikisano wa 4 NATIONALS TOURNAMENT mu mzinda wa Francis town ku Botswana kuyambira pa 28 mpaka pa 31 March chaka chino Watuluka.

Kuno monga ife kwanthu ndikuichemelera yamotoyi kuti Chinthuchi tibwele nacho kuno kumudzi🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼

Address

Chilomoni
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KUMA STAND posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share