04/09/2026
GABA WAKANA ZOTI ANAWINJA MWANA WA FORMER FLAMES COACH, PATRICK MABEDI — ANITA MABEDI
—Kwa miyezi ingapo, pa social media pakhala pali mkangano komanso mphekesela zak*ti wosewela mpira Gaba Mhango amawinjana ndi Madam Football (Anita Mabedi), mwana wamkazi wa mphunzitsi wakale wa Flames, Patrick Mabedi. Nkhaniyi inadzetsa debate kwambiri pa social media, pomwe anthu ambiri ankafunsa k*ti, “Kodi zoona zake ndi ziti?”
Koma dzulo, Gaba anafotokoza mbali yake ya nkhaniyi ndipo anakana kwa mutu wagalu k*ti sanamupakulepo Anita Mabedi. Iye anapitiliza kufotokoza k*ti munthu yemwe anali naye (kuzemberana) anali m’nzake wa Anita, osati Anita mwiniwake.
Komabe, Gaba anavomeleza k*ti sinali AI ,iyeyo ndi Anita anali pamodzi ndi anthu ena ankangocheza m’nyumba ndikumajambula ma clip apa TikTok, ndipo kenako anapsopsonanadi. Anamupatsa kiss yomwe iye anati anali “French kiss.”
Pakadali pano Anita akumamuyitana GABA k*ti Bro ndicholinga choti anthu mukhulupilire Kuti anthuwa sanakhalepo pachibwenzi olo ndi tsiku limodzi sadapangepo zausatana limodzi.